30/09/2023
Morning guyz ndapanga creat page for a reason, ndkudzwa k*t pali anthu omwe amafuna atapangilidwa process ya kyc account kmanoo mwayi sumapzka kmanso enanu ndi ma agent tnm kmanoo pa shop panu palibepoo ukadaulo wok*t m***a kumasegulapo ma sim card kmanoo smart phone mulinayoo kmanso mwina account yanu yosegulira ma sim mudayiwala pin yanu ndapa page k*t mavuto onse tidzithandidzana panopa ntchto yonse tidziyipanga mwaulele