Abwenzi

Abwenzi My pen dont only write, they speak 👄 😮
Truths For Men 👬

Anthu okonda Dancehall sakuvetsa ndipo Mafuso achuluka 👇Kuyambira tsiku lomwe (Lawi adakamba zoti akupanga Battle ya pa ...
12/03/2026

Anthu okonda Dancehall sakuvetsa ndipo Mafuso achuluka 👇

Kuyambira tsiku lomwe (Lawi adakamba zoti akupanga Battle ya pa stage Malinga Mafia anapephedwa kuti akapange nawo ndipo anavomeleza kuti akapezekako kuti akakutumule ana onse a hip hip-hop akawawonetsa kuti iweyo nde Fadda wa dzamba dzonse pa Malawi pano.

Koma chifukwa choti anthu anamupepha Lawi kuti ngati Malinga akapezeke kumaloko akuyenera kuti amuitanire oyimba a Dancehall anzake akamenye nawo Battle osati a Hip-hop ndipo zikuveka kuti Lawi atasikhasika wasakha Reggae and Dancehall PRESIDENT yemwe amatchedwa kuti (BLAST IMVAI) kuti akabandulane ndi Malinga pa stage

Koma Malinga atangonva phekesela yoti akabandulana ndi (Blasto Imva) osati IKK monga m'mene amaganizila Malinga Mafia wasitha maganizo ake ndipo wanenetsa kuti sakapezekaso kumaloko zimene zikuaonyeza kuti Malinga akumuopa (Blasto Imva)?

Koma Mafuso ochuluka ngati awa nde anthu akufusabe pa Social Media 👇

Kodi mesa Malinga amadzitama kuti iyeyo nde TATE wa Dancehall yaku Malawi, zomwe zimatathauza kuti palibe yemwe angamugwetse nde zitheka bwanji kuti chokha chongonva kuti dzina la Dancehall President (Blasto Imva lilipam'ndandanda wokamenya Battle iye ndikusitha maganizo kuti sakapezekokaso

Tidziti Malinga akumuopa Blasto kuti atha kukamuonongera mbiri?

Zimenezi ndizina mwa zomwe akufusana anthu okonda Dancehall komanso omwe amamutsata (Malinga komanso Dancehall President Blasto Imva) 🧔👲🧑‍🧑🧔

Ena akuwona ngati kuti mwina chifukwa choti Blasto wakhala akumudya Malinga m'ma Collaborations onse omwe akhala akumuna, Ndizomwe zampangitsa kuti Malinga akhale ndi matha.

Malinga amayesa kuti akaphana ndi IKK Mwatsoka wanva kuti akaphana ndi Chilombo Blasto Imva pompo wasitha maganizo kuti sapanga nawonso za Battle. 🙏

Munthu wina dzina lake (Mr Kruger) wamangidwa chifukwa choti nkhumba yake imodzi yabereka mwana wa nkhumba yemwe wabadwa...
11/03/2026

Munthu wina dzina lake (Mr Kruger) wamangidwa chifukwa choti nkhumba yake imodzi yabereka mwana wa nkhumba yemwe wabadwa ndi mawonekedwe ngati amunthu.

Apolisi anatenga zitsanzo za (DNA) wa Bamboyo kuti akaziyese. Ndipo zotsatira zake zinasonyeza 78%, zomwe zikuwonetsa kuti mwini wa Mwanayo ndi bamboyo.

Koma padakali pano zikuveka kuti apolisi akupitirizabe kufufuza za nkhaniyi.

Anawotcha Mwana Omupeza Ndipo tsopano wagwidwa ndi apolisi.Zachitika ku Kenya 👇Mwamunayu anakwatira nkazi oti ali kale n...
02/03/2026

Anawotcha Mwana Omupeza Ndipo tsopano wagwidwa ndi apolisi.

Zachitika ku Kenya 👇
Mwamunayu anakwatira nkazi oti ali kale ndi ana awiri. Koma patapita nthawi, anayamba kuzunza anawo chifukwa ankati si ana ake si ana amagazi ake. 💔😢

Nkhazazo zinayamba kukulira koma Mayi a anawo chifukwa chofuna kusamala banja am angoyang’ana zithunzo zikuchitika anawo akuzunzidwa koma osachitapo kathu masiku apitawo Bamboyo anatenga WAYA wa moti ndikuwotchawotcha thupi la m'modzi mwa anawo komanso sanathele pomwe anadulaso chala chimodzi chakuphanzi cha mwanayo. 😭

Ndipo atangopanga zimenezo anathawa koma atasakidwasakidwa anamuvumbulutsa pa chitsamba chomwe amabisala ndipo anamugwira moti Padakali pano ali m'manja mwa apolisi.

Zinthu zotere zimapweteka kwambiri… mwana wosalakwa kuchitilidwa nkhaza chifukwa chongosiya magazi ndi limodzi mwa kholo lake.

Ngati ukanakhala iwe mayi ake, ukanachita chiyani pa nkhani ngati imeneyi? 👇

Mtsikana Uyu ndiwaku Nigeria anasowa osamawonekaso m'mwezi wa December, ndipo akwawo akhala akumufunafuna komanso kumape...
01/03/2026

Mtsikana Uyu ndiwaku Nigeria anasowa osamawonekaso m'mwezi wa December, ndipo akwawo akhala akumufunafuna komanso kumapepha anthu kuti adziwathandiza kuyang'ana

Ndipo nthawi yomwe anasowa ndikuti atasiya Mwana wake wadzaka 5 koma Mwachisomo wabwelera yekha pakhomo koma chomwe chadabwitsa anthu ambiri ndichoti wabwelera pakhomopo ali ndi Mimba. 😮

Ndipo akuti sakuyekenza kuuza achibale ake zakomwe anali komanso zakomwe watenga pathupipo. 🙏

M'modzi mwa oyimba olemera kwambiri muno mu Africa yemwe dzina lake amatchedwa kuti "Tzy Panchak" wawotcha galimoto lake...
01/03/2026

M'modzi mwa oyimba olemera kwambiri muno mu Africa yemwe dzina lake amatchedwa kuti "Tzy Panchak" wawotcha galimoto lake la nyuwanu mu kanema yemwa amajambula masana a lero.

Galimotori ndi Galimoto lija lomwe liri mgulu la magalimoto odura kwambiri padziko lonse lapansi lomwe limatchedwa kuti "Lamborghini, yomwe ndalama zake ndi pafupifupi 388 million

Ndipo Phekesela zina zikuveka kuti oyimba wina waku Malawi yemwe amatchedwa kuti Charisma Madness atanva zimenezo anathamangira komweko ndikukamuletsa kumuletsa oyimba olemerayo kuti asawotche Galimotolo pomupepha kuti asithane ndi Galimoto la ntundu wa SIENTA kuti agwilitse ntchito pojambura Kanemayo, koma oyimbayo anakana ponena kuti zimenezo ndizazing'ono Galimotolo anagulira machenje. 😭🙏

Ndipo pamapeto pake oyimbayo anamuuza Charisma oyimba waku Malawi yo kuti akamamaliza kujambura nyimbo amulondore kunyumba kwake akamupatse "Lamborghini" yomwe imangokhala "ife tingoti Congratulations" Charisma madness pokhala artist oyambilira kuyendera "Lamborghini" pampanje ngakhale ili yogailidwa koma ndiyakobe. 🙏

Akazi ena amachita kusaweluzika podzigona okha kwa nthawi yayitali chifukwa chosowa Mamuna, kenako akapeza Mamuna wabwin...
01/03/2026

Akazi ena amachita kusaweluzika podzigona okha kwa nthawi yayitali chifukwa chosowa Mamuna, kenako akapeza Mamuna wabwino ndi owakonda, amayamba kumunena kuti sakuwakwanira. 😐

Izi zimachitika chifukwa choti akamaoeza Mamuna oti awakwatire amakhala kuti awonongeka kale ku Ndata komanso ena amakhala kuti anazolowera kudzigona okha kuteleko akamagonedwa ndi wina samanva bwino, zimakhala zovuta kuti anzawoyo awafikepo.

Kutero amayamba kumutchura Mamuna wawo mawu onyoza ngati “one minute man,” monga momwe "Tonto Dikeh" ankamutchura Mamuna wake wakale kuti "One Minute Man" chifukwa sankamufikapo nkaziyo anazolowera moyo omadzigona yekha.

M’malo movomereza zolakwa zake zakale, Amayimba mlandu Mamuna wosalakwa amene ali wachibadwa kuti sachedwa kutopa akayamba kugonana. Nkaziyo ankafuna Mamuna adzimugonabe olo atatopa, amayamba kufuna zinthu zopitirira malire.

Ena amati zimenezi zimayambitsachititsa:

kubadwa kwa ana osadziwika bwino abambo awo m'banja, chifukwa nkazi amasiya kukhulupirika.

Monga Mamuna, uyenera kumudziwa bwino mkazi wako usanapereke mtima wako wonse. Ngati akusonyeza zizindikiro zosakhazikika, uyenera kukoza vutoro msanga. Ngati uzinyalanyaza, tsiku lina ungadabwe ndi zotsatira zake ali pamwamba pa wina.

Osalowa m’banja ndi munthu amene ali ndi mbiri yochuluka yosakhazikika popanda kumvetsetsa bwino moyo wake.

“Had I known” nthawi zambiri amakhala mawu omaliza a munthu amene sanasamalire chisankho chake.

Woimba nyimbo wa ku South Africa, Master KG, potsiriza watulutsa zimene zinali mumtima mwake pa Twitter.Iye anati: “Sind...
01/03/2026

Woimba nyimbo wa ku South Africa, Master KG, potsiriza watulutsa zimene zinali mumtima mwake pa Twitter.

Iye anati: “Sindikufuna kunama, Makhadzi ndi mkazi wabwino kwambiri amene ndidakhalapo naye m'moyo mwanga. Ndipo ankandithandiza pondipanga pa sapoti nthawi zonse pa ntchito yanga ya mayimbidwe ndipo tikhala tikupanga nyimbo zabwino limodzi zomwe anthu ambiri ankazikonda. Koma vuto langa lomwe ndunathetsera ubwenzi wathu linali lakuti ndinkadandaula m'mene ana athu angadzawonekere. Koma patapita zaka ndaona kuti akufunukilabe m'moyo mwanga, ndikumufunanso m'moyo mwanga. Ndawona kuti Ma slay queen amangofuna ndalama zokha.” 😭

Makhadzi ataona izi pa tweeter po, anayankha mwachindunji kuti: “Wena Master KG, Siine woipa, ndimangofanana ndi bambo anga. Ndine mkazi wokongola, ndipo sindidzakulolanso kudzapsompsona nkhope yanga yokongolayi.”

Nkhaniyi yachititsa anthu ambiri pa social media kuyamba kukambirana ndi kugawana maganizo awo pa ubwenzi wa awiriwa. 🙏

Ku Nigeria, Mayi uyu amangidwa ndi apolisi chifukwa chozunza mwana omupeza.Akuti Mayiyo anayamba kumunena Mwanayo kuti n...
01/03/2026

Ku Nigeria, Mayi uyu amangidwa ndi apolisi chifukwa chozunza mwana omupeza.

Akuti Mayiyo anayamba kumunena Mwanayo kuti ndi mfiti nde Bambo wa Mwanayo atapita ku ntchito Mayiyo anatenga tsabola wa kapiripiri n’kumupaka thupi lonse kuphatikizapo kubibira.

Mayiyo akuti anachita izi pofuna kumuchiza Mwanayo akuti amafuna kuti (UFITI) omwe uli mwa, Mwanayo atuluke. 😭😭

Nkhaniyi yakhumudwitsa anthu ambiri chifukwa mwanayo ndi wosalakwa, ndipo zimene zinachitikazo ndi nkhanza. Pakali pano, mkaziyo ali m’manja mwa apolisi kuti afufuzidwe ndi kuyankha mlandu wake. 🙏

🚹 LISTEN UP,MEN....SUCCESS NOW BELONGS TO THE MOST FOCUSED, NOT THE MOST TALENTED. In this generation, it’s no longer ab...
01/03/2026

🚹 LISTEN UP,MEN....

SUCCESS NOW BELONGS TO THE MOST FOCUSED, NOT THE MOST TALENTED.

In this generation, it’s no longer about survival of the fittest.

It’s now survival of the most focused.

It’s now about who knows what they want, and refuses to be distracted.

You can be talented and still fail.
You can be smart and still stuck.

Why?
Because without focus, you’ll keep starting and never finishing.

Everyone is busy.
Everyone is trying.
But only the focused ones are building empires, creating impact, and making money consistently.

Focus is now the real currency.

So what’s stealing your focus?

EXTERNAL DISTRACTIONS

•Social media scrolling
•Endless WhatsApp chats and group messages
•Phone notifications every 5 minutes
•Unnecessary calls
•Excessive watching of movies
•Trying to keep up with every trend
•Consuming too much content without action
•Jumping from course to course
•Attending every training without implementing
•Always being available to everyone

INTERNAL DISTRACTIONS

•Overthinking and second-guessing
•Fear of missing out (FOMO) •Comparison syndrome
•Perfectionism
•Procrastination disguised as “planning”
•Imposter syndrome
•Emotional baggage
•No clarity or defined goals
•Trying to please everyone
•Saying “yes” to everything

LIFESTYLE DISTRACTIONS

•Poor time management
•No structure or routine
•Toxic relationships
•Multitasking everything, finishing nothing
•Inconsistent sleep or rest

If you want to win in this season,

Mute the noise.
Pick your lane.
Protect your focus like your life depends on it because it does.

The world is loud.

You don’t need to do everything.

You just need to do the right thing, and do it consistently.

P***S CARETake Care of Your P***s...Tips to keep your p***s clean, sweet and healthy.As a man, keeping your p***s health...
01/03/2026

P***S CARE

Take Care of Your P***s...

Tips to keep your p***s clean, sweet and healthy.

As a man, keeping your p***s healthy and sweet is important. Your sexual
organs are very valuable and must be cared for.

1. A clean p***s is very important so wash your p***s with warm water at
least twice a day. Clean the sc***um and under the p***s shaft gently and
scrub your scrotal sack too.

2. Leaving too much hair around the p***s is not cool, hair around the base of the p***s can be breeding ground for boils and cause bad odour so shave or keep it short and clean.

3. Don't pamper the p***s too much, As soon as you notice an infection, boil, rashes, please get help
immediately.

4. Many guys wear one boxer for a whole week or even a month but for health reasons pls change your
boxers everyday. Dirty boxer may give your p***s a permanent bad smell and a bad taste.

5. Guys what you eat affects the taste of your semen or pe**le juice. Avoid
too much garlic, onion, alcohol,coffee and spicy foods. Eat fruits that are
high in natural sugar like oranges, apples, mangoes and please take honey too. They all make your s***m
taste good to feed the egg for a healthy baby.

6. A woman's face may need makeup but not your p***s. Avoid using powder around the p***s. If you do,
especially after shaving, you might have to deal with serious irritations. The p***s doesn't need perfume to smell good so don't spray perfume around your p***s.

*NB*: For those who are not
circumcised, in your case, please pull back the the fo****in and wash underneath with warm water everyday.

Always remember, a clean p***s is mightier than Goliath's sword..

Finally guys, please go for a quick check up if you notice any changes within your sc***um, this could be a sign of prostrate cancer. It's common among men about and above 50years.....

Men, please this is educational material so don't take offence prostate cancer is real and claims life.


Address

Kauma Lilongwe
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Abwenzi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category