Sarf carldin

Sarf carldin Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Sarf carldin, Grocers, Lilongwe, Lilongwe Area 6.

Ex wanga akuti tibwerelane part  01 writting by sarf carldin.📝📝📝dzina langa ndine chisomo, lero ndakomana ndimunthu amen...
26/05/2026

Ex wanga akuti tibwerelane part 01 writting by sarf carldin.📝📝📝dzina langa ndine chisomo, lero ndakomana ndimunthu amene ndimagani kuti ndinamuiwala kale.anaima pa tsogolo panga,maso ake ali ndipempho lozaza ndichisoni"chisomo chonde.... tibwerelane.sindingathe kukhala opanda iwe".adatero Malick mawu Ake akugwedezeka.ndinangomuyang'ana ndipo mtima wanga unadupha chifukwa ndinakumbukila zonse zomwe anachita mbuyomu, ndipo sindinachitile mwina koma kungomuchokera basi.zaka zitatu zapitazo anandisiya popanda chifukwa choveka bwino.iyeyo anandiuza mbuyomu kuti wapeza mkazi wina ineyo ndingamuchedwetse, ndisaname ndinamufusa Malick, ndipo ndimangoganiza ngati angokamba zocheza koma ayi ndithu anali serious.adatuluka nyumba uku akuimba phone📱📱ngati bodza ulendo unali omwewo ndinakhala ndimafuso opanda mayankho ndisaname Malick adandisiyira misozi😭😭😭 ndipo zinanditengela nyengo kuti ndiiwale,koma pakupita Kwa kanthawi ululu unayamba kuchepa. Ndinayamba kukhala ndekha,ndinaphuzira kuzikonda ndekha ndipo pakanapano moyo wanga ulibwino.koma iyeyu wabweraso ndipo akukhala ngati palibe chomwe chinachitika ,kumuona Kwa lero kwandikumbutsa mabala ena. NEXT

Ex wanga akuti tibweranane part 1 ikuyamba mawa, writing by  sarf cardine
24/05/2026

Ex wanga akuti tibweranane part 1 ikuyamba mawa, writing by sarf cardine

21/04/2026

Ine ndilinawo mavideo Ake onse 0997099018 ndiponya popopo

Ndiyakhuleni guys iPhone 13 and nissan juke 099709918
30/03/2026

Ndiyakhuleni guys iPhone 13 and nissan juke 099709918

13/01/2026

Akut sizinali zovuta kulengeza kugonja kwa president chakwera

Car for sale in area 6 Lilongwe call me 0997099018
11/01/2026

Car for sale in area 6 Lilongwe call me 0997099018

Used car for sale in area 6 Lilongwe call me 0997099018
11/01/2026

Used car for sale in area 6 Lilongwe call me 0997099018

11/01/2026

Address

Lilongwe
Lilongwe Area 6

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sarf carldin posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category