LOYAL Charter

LOYAL Charter Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from LOYAL Charter, Grocers, Lilongwe.

13/05/2026

Koma boiz mupole moto
☝️☝️😂😂😂😂😂

I accepted 4 fan badges from John G Mandanda, Tamia ja and 2 others.
30/04/2026

I accepted 4 fan badges from John G Mandanda, Tamia ja and 2 others.

22/04/2026

In case you miss it 🙆🙆

Mkazi wina anayandikira mwamuna n’kunena kuti,Pepani bwana, ndikuchita kafukufuku pang’ono. Kodi ndingakufunseni mafunso...
24/03/2026

Mkazi wina anayandikira mwamuna n’kunena kuti,

Pepani bwana, ndikuchita kafukufuku pang’ono. Kodi ndingakufunseni mafunso?”

Mwamunayo anayankha kuti,
Inde, palibe vuto.

Mkazi anafunsa kuti,
Ngati mukuyenda pa basi, ndipo mkazi wina alowa koma palibe mpando woti akhale mungamupatse mpando wanu?

Mwamuna anayankha kuti,
Ayi.”

Mkazi anafunsanso kuti,
Nanga ngati mkaziyo ali ndi pakati, mungamupatse mpando?”

Mwamuna anayankha kuti,
Ayi.”

Mkazi anapitiriza kuti,
Nanga ngati ndi mkazi wokalamba, mungamupatse mpando?”

Mwamuna anayankhabe kuti,
Ayi.”

Mkazi anakwiya n’kunena kuti,
“Inu ndinu munthu wodzikonda kwambiri, mulibe ulemu! Mukuganiza kuti ndinu ndani?

Mwamuna anayankha modekha kuti,
Ine ndine basi driver.😂😂😂

Zeze is the godfather of AmaPiano in Mpanje and he has proved that he is here for the Long Run and he is going no where ...
19/03/2026

Zeze is the godfather of AmaPiano in Mpanje and he has proved that he is here for the Long Run and he is going no where anytime soon, he is here to STAY

He got a hot wife, his ex is Temwa, his cousins/uncles is GD & Marcus, he is bestfriend wit GABA, he got more than 10 legit hit songs, Ni**as Kno NOT to start smoke wit him, it’s jus a waste of time

When Fada Moti came in the Game wit “Mudyera” and then later dropped “Kutali”, I was one of those who really believed he was better than Zeze and he has replaced Zeze but fast forward in 2026 Zeze is still HIM while Fada is jus a WASHED UP artist like Rashley

So Jaa Kev and Charizma Kno Not to pin their artist Joe Icon against Zeze but to work him cuz Zeze is they father

So who is better opponent for Atate Joe Icon than Ntate Fada Moti

Right Now it’s Not a secret that Joe Icon has completely replaced Fada Moti in the AmaPiano scene interms of motion, hits and stage performances and I’m sure Fada is having sleepless nights wit the Mabvubvu guy

joe icon naming his EP “Atate” is not a coincidence, jaa kev knows what he is doing and they want to rub it in Fada moti’s face that Joe Icon is the real Ntate

The new 20 kwacha and 50 kwacha coins to be launched next month
17/03/2026

The new 20 kwacha and 50 kwacha coins to be launched next month

 Reserve Bank of Malawi yasintha ndalama za K50 ndi K20 kuchoka kukhala zapepala ndikuti zizikhala zachitsulo tsopano at...
17/03/2026



Reserve Bank of Malawi yasintha ndalama za K50 ndi K20 kuchoka kukhala zapepala ndikuti zizikhala zachitsulo tsopano ati kamba kakukwera mtengo opangira ndalama zapepala.

Gavanala wa reserve bank, George Patridge wanena izi ku Lilongwe, ndipo watsindika kuti izi sizikutanthauza kuti mphamvu za ndalamazi zachepa

Wolemba Kingsley Jassi

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LOYAL Charter posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category