Scholar Patrick nyoni

Scholar Patrick nyoni Scholar me sir

04/03/2026

Akhwaaka

26/02/2026

With Prophet Wisdom Jacob kamanga – I'm on a streak! I've been a top fan for 3 months in a row. 🎉

26/02/2026

I accepted 1 fan badge from Akhwaaka.

just see and pass
15/02/2026

just see and pass

Khalan oyera ndipo pempharan mseli
13/02/2026

Khalan oyera ndipo pempharan mseli

12/02/2026

samalani

02/02/2026

bekanipo Waka chonde

30/01/2026

I'm in the top 15% of Akhwaaka fans. I earned 81 points on their weekly engagement list last week.

my father
24/01/2026

my father

21/01/2026

Ndiye nthawi inayache amayathu otibala analoweza system yomati akalakwa mmodzi ati kumatikwapula tonse, amene sunalakwe iwe ukawafunsa kuti iye mundiphomolera chani? Nkesa walakwa ndi uyo? Amayankha ati mzakoyo akalakwa iwe uli kwani? Usakamulesa eeeh? Ndiye ndizikuswani nonse kumene chifukwa ndakuonani ndinu ana amatama, ndiye amakwapula mu akatumbamu, koma siku Lina titakwiya tinaagenda ndi duka koma kunachema kunali kuthamangisana, kuzungulira nyumba uku iwo akutokota akati nditamugwireyo ndimupha basi ife tikazati lerotu amama mutonama🤣

Address

Kamteteka FP School Box 157 Mzimba
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Scholar Patrick nyoni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category