Mwalizuku stories by Damazio Mnyayi

Mwalizuku stories by Damazio Mnyayi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mwalizuku stories by Damazio Mnyayi, Grocers, Mwalizuku village, post office box 79, Lilongwe.

18/03/2023

Hello guys, ndapanga tsambali ndicholinga Choti tizitha kupatsirana ndikudziwa nkhani zangochitika kumene mudera lathu ndicholinga Choti amene sakuziwa adziwe nawo komaso amene tili NDI ma business titha kumasasa

17/03/2023

Mwaswera bwanj anthu nose pamudzi pano, ine ndaswera bwino.

Tikulandireni alendo nose mwatijoina pamudzi pano mwachidule ndingot khalani womasuka.

Tiyeni titsate malamulo apamudzi pano, ndipo malamulo athu ali motere; 1. Tisatukwane 2.tisamatumize zolaula 3. Tikhale okondana Wina NDI mzake 4. Tilemekezane potsatengera msinkhu wanthu

Tionesese Kuti malamulowa tiwasatire aliyese opezeka kuphwanya malamulowa, lamulo lizagwira ntchito, kachikena ndikuti aliyese akhale omasuka.

Tiyeni tipasireni nkhani zosiyanasiyana zomwe zangochitika kumene mudera lathu ndi Zina zotero kupatula zotukwana, zikomo kwambir

Address

Mwalizuku Village, Post Office Box 79
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mwalizuku stories by Damazio Mnyayi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category