Lomwe information

Lomwe information Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lomwe information, Grocers, Kasungu chulu Kaliuli school Post 25, Lilongwe.

29/11/2025

Dpp yikuwona ngati 2030 silidzafika Ku Dpp kuli mbuli za ma minister

29/11/2025

Ogwira ntchito zaboma Anali busy kukavotera Peter nkhalamba lero yizi ntchito zayamba kutha ena kutsitsidwa pansi MDF kmso Ku police chibwana

19/11/2025

Pasuwa mpira sutelotu babatunde kmso singo Ku flames ai apeze zina zochita

18/11/2025

Dpp 2030 yidzaluza believe timayamba kuwona ma comment aanthu pa fb a dpp sapota akuchepa alimbili ndi owanyoza

27/09/2025

Dpp Achisale abwera kusokoneza anthu aku opposition koma opposition yake siyimeyi uyinva kuwawa

21/09/2025

Mcp bwana akanadya zaboma uja no worry

08/09/2025

Mtima wanga dekha akasikoyamba kuwona dpp yikuluza zisankho

02/11/2024

Manoma always kunvetsa kuwawa masapota Kodi nyimbo yija anayimbira yifetu a great Angels kwacha opanda Dipo ndafowoka

25/11/2023

Yife akufuna kutitumiza ku Denmark tikasamare ng'ombe zamkaka next month

Address

Kasungu Chulu Kaliuli School Post 25
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lomwe information posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category