Ngoli public business

Ngoli public business Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ngoli public business, Grocers, Lilongwe.

22/11/2025

morning everyone
mwa a mbuye

28/10/2025

kondowole pa theba
yesan zimenez yolowetsa 900,000 profit phwamwamwa tipange izi inbox

iziso timakwera
28/10/2025

iziso timakwera

25/10/2025

ndi season ya usipa ino tiyen tiyeseko kuja older tizigoba 20 kaya ndi 50 ndikusunga usipa umasowa minyezi ikubwerayi mbali ina tikupanga zina ndi zina

25/10/2025

pali geni zina sik*t zimalira ndalama zambiri kuyamba koma ngat kuli kotheka k*t makobidio alipooyambira tiyen tizicita k*tengera ndimmene mthumba kwathu muliri wa busines sadikira kapitolo yambiri

Sizinayende😥
20/10/2025

Sizinayende😥

Uyuyu ndiya nkhimba kuyamba kwake ndi simple kupanga makwacha zosalimbana ndukasokola mboni ndi gaga pakhomo basi kateme...
20/10/2025

Uyuyu ndiya nkhimba kuyamba kwake ndi simple kupanga makwacha zosalimbana ndukasokola mboni ndi gaga pakhomo basi katemera pang'ono zatheka tikulumikizitsen ndi musope mukafuna cetificate k*ti mukhale ndi ukadaulo ose tiyankhulane tikulumikizitsen ndi msope nkhimba ndi dilu

20/10/2025

Business ndiyose bola pakubweretsera khobidi osasankha😊 Zikuveka achina ujen kumeneko

20/10/2025

Chiyambi chabwino pa malonda ndikudzi funira kapena mundiganizira zabwino pa iwe mwini ( high self-esteem) zimene zimakupangitsa kukhala olimbika nthawi zose tidziwe zambiri like and follow Ngoli public business

Nde subject let's follow and share toothers k*t zisakuphonyen
20/10/2025

Nde subject let's follow and share toothers k*t zisakuphonyen

13/10/2024
13/10/2024

Ntchito ya kafesedwe ka mitengo
Kuchita ndi kuphuzira ndondomeko za kafesedwe kabwino ka mitengo.
Njira yoyamba ndi kukoza malo offeseramo mitengo yanu k*t ikhale yosamalika
Yachiwiri ndi kusankha dothi loyenerer " tingalidziwe bwanj? Ili ndi dothi lomwe liri ndi nthaka
Yachitatu kapakiridwe koyenera mma tude onetsetsan nthawi yomwe dothi lanu likulowa mu tude rilibe mwala kapena pepala ririrose la plastic.
Izi ndi zina mwa zomwe mungachite pa kafesedwe koyenera ka mitengo.

Like and follow this page ngati mukufuna kuphuzira zambiri put your idea in comment section.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ngoli public business posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category