Jackison yohane leven

Jackison yohane leven Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Jackison yohane leven, Grocers, Lumbadzi near airport, Lilongwe.

So sad
03/12/2025

So sad

03/12/2025

Kodi mumadziwa izi๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
Kalekale galu๐Ÿ•ndi nkhanjwe๐Ÿ… zimakhala kumanyumba zonse pamodzi zidali pachizake chenicheni tsiku Lina galu๐Ÿ• adapita kukaba mazila๐Ÿฅš๐Ÿฅš๐Ÿฅškumudzi wina wakutali alikumeneko kokabako anthu adayamba kumuthamangitsa galu adayamba kulila ngati mzake uja nkhanjwe๐Ÿ… atafika kunyumba galu๐Ÿ• adatenga mazila ๐Ÿฅš๐Ÿฅš๐Ÿฅšaja ndikuwaphika zigoba zake nukaziponya kogona kwa nkhanjwe๐Ÿ… momwe kumacha anthu adabwela kunyumba yankhanjwe ndikungoyamba kuyimenya nkhanjwe idafusa kuti zatani anthu adati iwe wakuba udaba mazila๐Ÿฅš๐Ÿฅš๐Ÿฅš๐Ÿฅš zigoba zake ndi izi nkhanjwe adayithamangitsa kumudzi kuti isadzapezekeso galu adayamba kukondedwa koposa ,
Masiku anowa Pali anthu ena Ali ndi mtima okhala ngati agalu ๐Ÿ•๐Ÿ•aja amanena mabodza kwa okondedwa wanu ndicholinga ayambe kukondedwa iwowo kaya ku ntchito kumene alipo anthu amtima ngati wagalu chonde apeweni amenewo
Pangan follow page iyi

uyu ndi dolo link ili m,musimuPali iyi akuti liva yi oho... Its the concept for me, ๐Ÿ™Œ๐Ÿ”ฅ
03/12/2025

uyu ndi dolo link ili m,musimuPali iyi akuti liva yi oho... Its the concept for me, ๐Ÿ™Œ๐Ÿ”ฅ

This new track carries a deep and emotional message a reflection on depression, and how many people turn to alcohol when the pain becomes too heavy. The song...

03/12/2025

Mwawuka mbwanji nonse

28/07/2025

Awa ndima websites omwe mungagwilitse ntchito kupangila dawunilodi ma series ndima movizi mwaulele koma abwino. Ambili amagwilitsa ntchito ma websites amenewa.

1. FZMovies

2. ToxicWap

3. NetNaija

4. MKVMoviesPoint

5. HDMovie2

6. 9xMovies

7. Series9

8. KatMovieHD

9. MoviezWap

10. MoviesVerse

Yoonjezera
Movie box

For education purposes only

13/05/2025

NGATI MWA BELEDWA

Pezani zinthu izi

1. loaf ya bread osadula ๐Ÿž
2. Adyo ๐Ÿง„
3. Ufa otsalira pa mafuwa
4. Khala (charcoal)
5. Teaspoon ya mafuta akhumba

Yatsani moto, wakuti uziyaka monga kuyatsa nkhuni, ma plastic, zikatoni or zinyalala.

Zikamayaka, Tengani chinthu chimodzi chimodzi ndikumaponya pa motopo motsatizana,

Pamene zikuyaka, muzinena mawu amene mukufuna kuti wakubayo apange or zimchitikile, kaya mukufuna kuti katundu wanu apezeke, kaya mukufuna awonongeke asagwilitseso ntchito, kaya mukufuna wakubayo ayende mmatembelero, kaya mukufuna kuti wakubayo agwidwe, zilankhulani zimenezi pamene zinthuzo zikuyaka.

Mukhoza kupanga nthawi iliyose mmawa masana or madzulo.

Note: ngati mukufuna katundu wanu obedwa abwelele or apezeke, onetsetsani kuti muli dela lomwe katunduyo anabedwela.

Ngati munabeledwa ndi amaliongo ma dobadoba akuti nawoso anaiwala kuti anakubelani, ndiposo katunduyo anatayitsa kalekale kuti apeze yomwela, onetsetsani kuti muli dela lomwelo.

Pangani izi ngati mwabeledwa pasanathe miyezi itatu. Ikaposa apo ma chances amakhala ochepa.

Zikomo

05/05/2025

*VUTO LA MWELA / PHUZI (HERNIA)*

๐Ÿ‘‰ Awa ndi matenda omwe amapangitsa kuti mabatile azibambo kapena mnyamata alowe mkati komanso angakhale mwana wang'ono amadwalanso chimodzimodzi

*NJIRA ZA CHILENGEDWE ZOTHANIRANA NDI NTHENDA YA MWELA*

*NDONDOMEKO YAKAPANGIDWE KAKE*

*1)๐Ÿ‘‰ Pezani mtondo.*
โ€“ Tengani mandimu asanu kuwaduladula ndikuponya mu mtondomo
โ€“ Adyo musanu
โ€“ Aluvela musanu
โ€“ Mizu ya mtengo wa pawpaw chikhatho chomodzi.
๐Ÿ‘‰ Zonsezi muponyere mu mtondo musinje
Kenako ziyikeni mu mpoto mutereke pa moto kwa mphindi khumi ndi zisanu muli madzi okwanira 10 litres
๐Ÿ‘‰) Sefani ndikusunga malo ozizira bwino
*DOSAGE YAKE*
Muzimwa katatu patsiku pogwilitsa ntchito kapu yaying'ono ya tea kwa sabata

*2). Black seed oil or powder"*
๐Ÿ‘‰ Pezani kalonji oil kapena kuti black seed powder (imwani kwa ma week anayi or kuposera apo kawili patsiku komanso pezani neem oil muzipakapo

*3). Masamba a Chitimbe"*
๐Ÿ‘‰ Pezani masamba a mtengo wa chitimbe mubwatitse muzimwa madzi akewo katatu patsiku mpaka mutaona kusintha.

*4). Mabilinganya"*
๐Ÿ‘‰ Tengani mabilinganya, nkuwaduladura nkuyika m'madzi ndipo muzimwa madziwo pafupifupi kwa tsiku lililose mpaka masabata awiri.

Address

Lumbadzi Near Airport
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jackison yohane leven posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category