Man Osman D

Man Osman D Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Man Osman D, Grocers, Malawi liwonde, Liwonde.

04/04/2026

Good morning my friends

13/11/2025

Mwadzuka bwanji pipoz

Send a message to learn more

20/08/2025

Good morning pipoz

Komatu akuluwa abvuta kobas
14/08/2025

Komatu akuluwa abvuta kobas



Mtsogoleri wa chipani cha Odya Zake Alibe Mulandu Dr. Micheal Usi, wabwereza kunena kuti m'boma mwachuluka anthu omwe akuba.

Dr. Usi omwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino anena izi m'boma la Phalombe pa msonkhano oyima-yima.

Malinga ndi a Usi, iwo ayima pa chilungamo ndipo sakuwopa wina aliyense ndipo akudziwa kuti pali anthu ena omwe akufuna kuthana nawo powamanga.

Iwo ati sanabe kanthu m'boma ndipo ndiokonzeka kuti anthu awafufuze ngati aba kanthu m'bomamu.

"Sindikuwopa, mundifufuze ndi mphuno momwe," atero a Usi.

(by Ronnex Chiwanda -Phalombe:08/14/25)

14/08/2025

Good afternoon ma guz madzulo Anu akuyenda bwanji kumeneko Kuno aaaaa kupanga Alihamudulilla alibwinoso ndithu kuyamika bas

13/08/2025

Mukavota mwachibwana pa 16 September pa mudya chiteze Kwa 5 years inaso

11/08/2025

🤣🤣

11/08/2025

Kusesa mumakuthawa Ku primary school kunja Lero ndizomwe tikudyela nazo Dollah pa theba pano🤣

Address

Malawi Liwonde
Liwonde

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Man Osman D posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category