Beans Farming ndi Mbewu zina zaku dimba

Beans Farming ndi Mbewu zina zaku dimba Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Beans Farming ndi Mbewu zina zaku dimba, Grocers, Mangoch, Monkey Bay.

07/04/2026
mavuto achiwawu amafunikaso kukomzekera tisanayambe za ulimizo
23/03/2026

mavuto achiwawu amafunikaso kukomzekera tisanayambe za ulimizo

21/11/2025

Alimi anzanga thawitu yolima nyemba ija ndiinoyi mukhoza kudzala chimanga ndi nyemba zomwe pokolora ndekuti mudzakolora zithu ziwiri zopindulits,,,Komano nyemba zanu ngati zili zoyanga mudziyesetsa muyambe mwadzala chimanga chenako nyemba koma ngat ziri zosayanga mukhoza kudzala tsiku lomwero

Kumalima mwina mkudzasimba lokoma tsiku lina
15/09/2025

Kumalima mwina mkudzasimba lokoma tsiku lina

Kumaonetsetsa pogula fertilizer ,,,uyu ndi wa Fake
15/09/2025

Kumaonetsetsa pogula fertilizer ,,,uyu ndi wa Fake

15/09/2025

Kumalimatu kumeneko

23/06/2025

Ulimi wanyemba ndiosavuta khani kungotsatira malangizo ndi ndondomeko zake
(1)spacing
(2)insecticides
(3) booster
(4)moisture content

Spacing ndi 10 by 20cm
Insecticides pa week kamodzi komanso achiwawu
Booster pa 2weeks iliyonse
Chinyezi chidzikhala cha size chisamachuluke kwambiri komanso chisamachepe ,,,

Tipeni ma customer  ozifuna nyembazi
22/06/2025

Tipeni ma customer ozifuna nyembazi

Khobwe 1300k pa kg
20/06/2025

Khobwe 1300k pa kg

20/06/2025

Nyemba is 3000 pa kg Kwamene akufuna

Address

Mangoch
Monkey Bay

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Beans Farming ndi Mbewu zina zaku dimba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category