Wintoo inter

Wintoo inter Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Wintoo inter, Grocers, .

27/10/2025

ELI Njuchi

21/10/2025

🧠💔Sayansi yapeza kuti azibambo a nzeru kwambiri zachikondi zimawavuta.

Akuti izi zili chomwechi kamba koti azibambo a mtunduwu amaganiza mozama kwambiri, chinthu chilichonse amachiwunika mwakuya asanachipange komanso amalemekeza ma ubwezi okhala ndi tanthauzo lenileni osati zinthu "zopanda pake" monga maonekedwe.

Iwowa tizoyankhula topanda pake amabhoweka nato. Zomati daily "ukutani? Wadya cha? Nduwoneka bwa?" zimawanyasa.

Mukamayankhulana nawo, amafuna nkhani zenizeni zoti akamakamba mutu uziganiza. Zinthu monga dating kwa iwowa nzopanda pake.

Ambiri mwa iwowa akuti amaopanso kwambiri ma rejection, ma "heartbreak".Azimayi dziwani zimenezo

Forgive our children 👨‍👩‍👦‍👦 please my God sizoona izi tingoti rest in peace kwa onse aluza moyo tsiku la lero 😭😭😭
15/10/2025

Forgive our children 👨‍👩‍👦‍👦 please my God sizoona izi tingoti rest in peace kwa onse aluza moyo tsiku la lero 😭😭😭

13/04/2025

. KWA AZIMAYI NDI AZIBAMBO

Banja likamavuta vuto ndi zinthu ziwiri basi Kumvera, kukonda Mamuna akonde nkazi amvele zikuvuta pati??

Azibambo ziwani izi mukangokwatira simukhalaso Moyo wanu koma mumakhalira yemwe mwamubweletsa panyumbapo, choncho inuyo ntchito Yanu ndikukonda basiiiiiiii, munthu yemwe mumamukonda ,umamuteteza,kudyetsa,kumveka, ndi zina.

Azimayi zimavuta pati kumvela? Ngati mukuona kuti simukwanitsa inuyo kukhala pansi pa amuna anu mukutaniko kubanjako? Velani amuna Anu muzonse sutsani mwa mzelu. Zikomo kwambiri.

MABANJA ALIMBE!

29/09/2024

Mary Nkhamanyachi Chilima writes

29th September was our wedding anniversary.

Ndikupempha nonse okhudzidwa kuti mundithandize kumema kafukufuku wapadera, kuti timve tsatanetsatane wa zomwe zinachitika pa 10 mpakana pa 11 June.

ANA OPEZA AKUKUMANA NAZOTU HUUUUU
28/08/2024

ANA OPEZA AKUKUMANA NAZOTU HUUUUU

20/08/2024

Kwa mwadxama uko Zikuti bwanji kod

Follow this page guys
20/08/2024

Follow this page guys

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

18/08/2024

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Wintoo inter posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Grocery Store?

Share