Kufooka kwa nkaz super story

Kufooka  kwa nkaz super story Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kufooka kwa nkaz super story, Grocers, Zomba.

18/01/2022

Choyamba pangan like kt nkhaniyi isakuduse .......Tsiku lina Ku school yathu kunali cultural day anthu amavala zomwe amalakwao kamat eeee mercy anavala modabwisa kwambiri ndipo ananditenga mtima. Ine chosaziwa kt nkazi ngakhale anali wakulu amandifuna . kuopa Kwa ine kumachitika chifukwa amakonda kucheza ndi anyamata akulu oposela nsinkhu wanga .km tsiku ili ndinamuitana mercy ndikumuuza k*t, congratulation for ur dressing my friend, end ur looking beautiful iye amayankha k*t thanks km zinali zomudabwisa Kwa coz macheza anthu anali ama diss kanali ngat koyamba ine kumuyamikila ,ndipo aziwa kt palinkhan .itafika nthawi ya break,mercy anandiuza k*t ndimupelekeze Ku grocery komwe tinakumana boyfriend wake wakale mmmmmm ine chosaziwa gyz k*t kunja kulinji .titangofika pamalo ena omwe playing ground ya Ana apa school yi ndinangodabwa khoofi pasaya panga ,ine kulephera ndalakwa Chan gys ,timakukhumba iwe sungamayende ndi girlfriend waine,anatelo mathews uku akuvula mayala ake. kenaka mercy anaima kusogolo kwaine ngat akunditeteza ,nde chikukukhuza ndichan mesa iwe ndiine chibwez chinatha ,unkaona ngat kuchoka Kwa kulibe wina ,atelo mercy akundikumbatila...............chonde gyz mundisangalase k*t naneso ndikusangalasen ,pangan like kt part 3 isazakudusen

13/01/2022

Choyamba pangan like k*t nkhan iliyonse isamakuphonyen...... Zona langa ndi Steve nkhan yanga yachikond inayamba ndili standard 7 ndinkaz yemwe anali best friend wanga zina lake mercy. Mercy anali nkaz okongola kwambri ndipo amaponderera school yonse, eeeee ndinalephera kupilira, km ndimakanika kufusila chifukwa mercy anali wankulu kuposa ine. Pomweso anyamata ena amamufunaso, nde zinali zondivuta kt ndimuuze zomwe ntima wanga umafuna.... Tiyen tidikile part 2 Sunday chonde ine ndikusangalasen inuso mundisangalase....... Watssap group number 💯 0990130217

Address

Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kufooka kwa nkaz super story posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category