Îmřăãň ¥ūšūf

Îmřăãň ¥ūšūf Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Îmřăãň ¥ūšūf, imraanyusufu0@gmail. com, Zomba.

06/01/2026

uli ngat chakatapila chokhoza nseu ukatheka tsichiloledwa kudutsa

uyenda bwanj uli oyuzidwa tsungadutse 😂

31/10/2025

Ukudzemba mkaz wako kapena mkaz kudzemba mwamuna wake or kudzemba makolo kupta k*tali kokakumana otsaiwala kudzemba Allah nd Angel

Mashaa Allah. Allah apitilidze  kukuongeleran Muft 🤗😍💦💦
24/10/2025

Mashaa Allah. Allah apitilidze kukuongeleran Muft 🤗😍💦💦

21/10/2025

PIZZA UJA AMAKOMA KOMA MGAIWA ODYA NDI MUTHU WOTI AMAKUKONDA ZEN ZEN UJA MULI UTHENGA 😜😜

Mtumiki muhammad (saw) anat Zina mwa zizindkiro za k*tha kwa Dziko ndko kupanga banja poyela athu akuona........Pakadali...
18/10/2025

Mtumiki muhammad (saw) anat Zina mwa zizindkiro za k*tha kwa Dziko ndko kupanga banja poyela athu akuona........

Pakadali pano mu dziko la south africa kuli azungu omwe aika mipikitsano yotsiyana tsiyana umoz mwa iwo nd kuyenda mbulanda kumadela monga ma school 'mall, kumapiri,kunyanja ndkuma taxi deport nd malo ena ndpo oyenda kwa 1hour iliyonse azipatsidwa R700 yomwe malawi kwacha nd 175000 malinga nd rate pakadali pano ndpo pak*tha pa mwezi nd R25000 ndye k*t pali bonus ya 4000 yomwe malawi kwacha ili 6 point chak*t million ndpo malinga nd malipot ampikitsanowu ak*t athu amene anakayenda ku forest ina amachita paja uku mkumajambulitsa.

Tili ku malawi wina aliyense amene ali nd phone ya smart kapna laptop ndzina zotero akuzwa k*t pakadali pano Atsikana ali busy kujambula maliseche awo mkumaponya pa social media ndcholinga chofuna k*tchuka nd zina zotero ngakhale mukawa funsa aziyakha mwa manyaz k*t mwina ndachta kupangidwa chpongwe nd mwamuna km zoona zake ndzot amachta Dala ndpo iwo ndi amene ak*tumikira shaitwan/satana ndpo satana akungokwanilitsa zomwe zinalakhulidwa kale

Thawi zonse tizimupepha Allah k*t atitalikitse ku ndale za satana

14/10/2025

Thawi zonse kumayamika mtendele wa Chisilam���

Tichosen umbuli ichi mumachitcha k*ti Chan?🙈🤦‍♂️🤦‍♂️🤣
01/10/2025

Tichosen umbuli ichi mumachitcha k*ti Chan?🙈🤦‍♂️🤦‍♂️🤣

01/10/2025

zamvekaso k*t plann yokwela mafuta inalipo ndkale linangotsala tsiku APM zake tsanayambeyi

Muli uthenga mu pic iyi chikond❤ cha amay Mulungu adalitse makolo athu tonse 🤲
01/10/2025

Muli uthenga mu pic iyi chikond❤ cha amay Mulungu adalitse makolo athu tonse 🤲

01/10/2025

Mwat Khan ya mafuta ik*t bwanj ?Amalawi ndye mwati timulumbilitsedi atisunga uyu
😫😫😫

Address

Imraanyusufu0@gmail. Com
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Îmřăãň ¥ūšūf posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share