Pastor Gama manyozo kapolo wa ambuye

Pastor Gama manyozo kapolo wa ambuye Informações para nos contactar, mapa e direções, formulário para nos contactar, horário de funcionamento, serviços, classificações, fotos, vídeos e anúncios de Pastor Gama manyozo kapolo wa ambuye, Mercearia, Milange sede, Milange.

14/04/2026

Good morning members

14/04/2026

Tiziyamika pa za bwino zimene chauta amatichitila pa moyo wathu mwana wosayamika pa zabwino zimene makolo amuchitila makolowo amakhumudwa

11/04/2026

Ife ND nyale yowalisa dziko chonde akhristu oyera mtima tisalore k*t mafuta atithele yehova akumane ND chotsowa chanu madzulo ano

22/01/2026

1Yehova ndiye kuunika kwanga ndi cipulumutso canga; ndidzaopa yani?

Yehova ndiye mphamvu ya moyo wanga; ndidzacita mantha ndi yani?

21/01/2026

Ambuye mukhale nafe usiku uno musalore satana atenge gawo pa moyo watu Amen

21/01/2026

Yehova anakulenga ND cholinga ndipake uli ND moyo

17/11/2025

Yehova akadzati uyu akhala apa palibe angeletse

29/06/2025

Yehova ND wachifundo amatisunga ndi moyo ngakhale tikumulakwira tsiku ND tsiku samawerengela m'phuluphulu zathu ndichifukwa chake tili ND moyo lero amen

10/06/2025

Lazaro anawukitsidwa kwa akufa iwenso nyengo zako zimene zinafa ziwukisidwe munzina la yesu

30/05/2025

Ndipezeni ku WhatsApp pa number iyi 258860275052 kukuchitika zozwizwa zadzikulu motsogozedwa ND mphanvu ochokera ku south Africa lowani malo asanathe

27/05/2025

Mwaswera bwanji okondedwa mwa ambuye ku WhatsApp kwasala Malo ochepa chitani changu kulowa Malo asanathe ambuye akudalitsen amen

24/05/2025

ukamalimbana ND anthu ena chifukwa Cha madalitso awo yehova amakusisabe mwayi wako umapita kwa amene ukulimbananawowo

Endereço

Milange Sede
Milange

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Pastor Gama manyozo kapolo wa ambuye publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Atalhos

Compartilhar

Categoria