Amos's exodus .mawu a Mulungu

Amos's exodus .mawu a Mulungu Informações para nos contactar, mapa e direções, formulário para nos contactar, horário de funcionamento, serviços, classificações, fotos, vídeos e anúncios de Amos's exodus .mawu a Mulungu, Mercearia, Kasapaila mozes, Vila Moatize.

11/05/2024

Odola omwe akusautsidwa chifukwa adzaona Mulungu

Send a message to learn more

11/05/2024
11/05/2024

Mawu a Mulungu Ali ndi mphavu yosintha kalikonse .pa nthawi yomwe tili mavuto tiyeni tizikhulupililq kuti mavutowo atha

11/05/2024

Abale anga tiyeni tiphunzitsane mawu a Mulungu omwe akuchokela pa

Aefeso 6:17 _ mutengeso cisoti ca cipulumutso. ndi lupanga LA mzimu ndilo mawu a Mulungu .
Abale anga ndimafuna kuti tilimbikitsane kuti mawu a Mulungu Ali ndi mphavu yosintha moyo wathu ..bale ndikuti mawu a Mulungu ndi chida choopsa kwambili pofuna kugonjetsela satana ..ngati tikufuna kuti tipambane mu nyengo kapena kuti nkhondo tikuyenela kusunga mawu a Mulungu chifukwa kutsogoloku mawu a Mulungu adzasowa ndiye pakufunika kuti mawu a Mulungu azikhala nu mtima mwathu ..lupanga LA mzimu ndiwo mawu a Mulungu tiyeni tiyesese kukhala anthu osunga mawu a Mulungu ...Amen

Endereço

Kasapaila Mozes
Vila Moatize

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Amos's exodus .mawu a Mulungu publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Compartilhar

Categoria