Zochitika kwa Mponya, Fodya, & Khokhwa

Zochitika kwa Mponya, Fodya, & Khokhwa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zochitika kwa Mponya, Fodya, & Khokhwa, Grocers, Blantyre.

10/01/2026

Sad 😭
SHOP ya Eliya (Jamahn) yabedwa dzulo usiku ndi anthu osadziwaka abamo katundu onse..

01/11/2025

omwe tikuwadziwa Mai live July Kwa mponya pafupi ndi ground la mponya atisiya lelo ku chipatala chichikulu boma la Chikwawa 😭😭zimu wao ukause mutendele

01/10/2025

Ndiye kuli azibambo okakamila wagisa. Kulikuthawa maluzi pompanda wagitsa mungakhale ndani inu. Azanu akupanga business inu machende gwee kumazinamiza kuti ndinu ma comment 😂😂😂 popanda wagitsa munakanakhala ndani ma bongwe inu ife timasakatu zithu ndi Maja athu inu siimwai wagisai munakanakhala otuwa simukusithikaso ai zovala zake zomwezo.. tiyeni pa ground 0 Kwa 100

17/09/2025

Welcome nonse omwe mwapanga follower page ino

Address

Blantyre

Telephone

+265996852384

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zochitika kwa Mponya, Fodya, & Khokhwa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category