Voogue

Voogue Business

21/06/2025
23/04/2025

PHWEDO.

ZINTHU 23 ZOKHUZA PHWEDO ZOTI MUDZAWASIMBILE ANAWO.

1.Dzina lake lenileni ndi : Tumpe Nigel Mtaya.

2.Anabadwa pa: 28 December, 1993.

3.Nickname yake ndi: Anundwe (m'buyomu anali osewera mpira ndipo anzake anamupatsa dzinali)

5.Zaka:32

6.Pa nkhani ya banja: Ngosakwatira

7.Nambala ya ma Ex-girlfriend ake: 3

8.Maphunziro ake okwera kwambiri: Diploma In Professional Journalism and Media Studies

9.Ntchito yomwe amagwira: Freelance Journalist and Videographer

10.Chakudya chomwe amakonda: Mpunga ndi mtundu wa ndiwo zilizonse.

11.Zokonda zake: Kusewera ndinso kuonera mpira, kuonera kanema, kucheza ndi anthu.

12.Team ya mpira yomwe amakonda: Arsenal, Nyasa Big Bullets ndi Real Madrid.

13.Osewera mpira yemwe amam'konda zedi: Cristiano Ronaldo

14.Chamba cha nyimbo chomwe amakonda: Nyimbo za zamba zonse.

15.Oimba yemwe amam'konda: Dirty Flow ndi K2b block clue.

16.Filimu yomwe amakonda kwambiri: Predator

17.Opanga mafilimu yemwe amam'konda: Arnold Schwarzenegger

18.Malo amene amamusangalatsa ku Malawi: Kawale

19.Filimu yomwe waonekamo: Mafilimu awiri (School Days komanso Where my Heart belongs) ,enawo sanatuluke.

20.Tsiku lomwe anakondwa kwambiri: Ati anakondwa atangobadwa kumene.

21.Tsiku lowawa m'moyo mwake: Mai ake atamwalira pa 20 December, 2023.

22.Chokhumba m'moyo wake: Kudzakhala opanga mafilimu osainidwa ku Hollywood.(American movie industry)

23.Kodi amasuta?: Ayi sasuta.
Kodi amamwa mowa? Inde amamwa mowa.

24.Scene imene inamusangalatsa kupanga act mu filimu ya School Days?:
- Ma scene onse.

09/02/2024

HELLO FAM

Send a message to learn more

Address

Chimwalira
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Voogue posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category