01/10/2024
Pano mitu siikugwira ayi. Akuyesela kuupukusa km opanda nyanga. Nkhani ndi mwana wa miyezi itatu. Akulira mosaneneka akayamba kulira akumakana chilichonse. Andifunsa ine chothandizo Cha momwe angamuthandizire mwanayo ndangowauza kt apite kuchipatala km akt apita koma sakupeza Vuto. Kupita kwa asing'anga sakupeza Vuto kumapemphero akumati akabwerako zikumayambikanso ndiye athandizeni a neighbor anga. Anzango omwe mukudziwa zochita please help me