Watipatsa Fisheries

Watipatsa  Fisheries TIMAPEZEKA NDI NSOMBA ZA LAKE MALAWI MONGA Chambo,Usipa, Micheni, Ndunduma, Kampango, Bombe ndi Milamba. ZAMOZAMBIQUE MONGA Makelere,ndi Zambo.

Zonsezi pamintengo yotchipa

05/01/2022

MONI MA CUSTOMER ATHU NONSE

Zikom pokhala nafe muchaka chathachi Ambuye akudalitseni

Ife A watipatsa Fisheries popitiliza kukupasilani Nsomba Zabwino zafresh,tadzanso ndinkhani yabwino kwainu k*ti Tayamba kupezekanso ndi ma Chicken pats pamimtengonso yabwino.

Kotero pamene mukubwera kumashop athu dziwani k*t muzikapezako mitundu iwili yazakudya.
*Nsomba za Fresh mitundu yonse

*Chicken pats ya fresh osati yokhalisa mu fridge

Tikukufunilani zabwino zonse pamene mukupitiliza kukhala macustomer athu,timakunyadilani

Ife tili pano kukupatsilani katundu wabwino ndi wotchipa

IFE A WATIPATSA FISHERIES TIKUMAPEZEKA NDI NSOMBA ZA FRESH ZOCHOKERA MUNYANJA YATHU YACHIMALAWI(Lake Malawi) MONGA:*Cham...
18/11/2021

IFE A WATIPATSA FISHERIES TIKUMAPEZEKA NDI NSOMBA ZA FRESH
ZOCHOKERA MUNYANJA YATHU YACHIMALAWI(Lake Malawi) MONGA:
*Chambo
*Micheni
*Milamba
*Ndunduma
*Usipa
*Bombe ndi zina zambili.
Kuonjezera apo munthuyu wandisiila
Zonsezi pamitengo yabwino.
TIPEZENI KU SHOP YATHU PA CHEMUSSA,BLANTYRE KAPENA KUNGOIMBA OR WHATSAPP PA +265991176474
Muzathandizidwa mwachikondi ndiimwasangala

Address

Watipatsa Fisheries C/O Blantyre
Blantyre

Opening Hours

Monday 07:30 - 19:00
Tuesday 07:30 - 19:00
Wednesday 07:30 - 19:00
Thursday 07:30 - 19:00
Friday 07:30 - 19:00
Saturday 07:30 - 19:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Watipatsa Fisheries posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Watipatsa Fisheries:

Share

Category