Spim vallihar

Spim vallihar 𝐓𝐢𝐰𝐞𝐥𝐞𝐧𝐠𝐞 𝐧𝐤𝐡𝐚𝐧 𝐳𝐚 𝐡𝐨𝐭 𝐩𝐚𝐧𝐨 ☑

25/03/2025

PEPAN KWA AMENE MUMANDISATILA NDIKULETHELA KUKEMBA NKHAN MUNTHU MABIZY KOMA OSANDITULUKA NDIKAZAPEZA MPATA BWINO BWINO NKHAN ZIZAYAMBA KUKUPEZANI BASI...PEPANI ONSE ZIKOMO😭

17/03/2025

💔CHIKOND SAYESANA💔
part 3.
pangan follow page.
atamuona mtsikana uja mtima wake unasika atapeza k*ti anali happiness apa ndipamene ananyamuka kumapita kwawo koma ali munjila anaganiza zomuimbila phone Hanah koma siimapexeka ndpo anangozisiya anayenda mpka kukafika kwawo.

Hanah ataona k*ti masautso sakumulabadila anangoganiza zopeza mamuna wina k*ti azimvana naye bwino bwino koma amasowa k*ti angamutulukile bwanji masautso basi anangoganizo zoti azingomudyela pot mzake anamuuza kale plan.

maria atafikwa kwawo anakalipidwa nd masten ake k*ti bwanj wachedwa ku msika koma chifukwa chak*ti maria anali ochenjela pakamwa anazibakila ndikuwanamiza mai ake aja mpka kukhulupilila ndithu.

nthawi itakwana 6 koloko maria anatenga makope ake ulendo waku prep(kowelenga) ku school koma ali munjila anazamva kuita munthu mbuyo mwake apa anatembenuka anapeza k*ti anali Hanah ndipo hanah anangofikila kumumenya nkhof maria apa maria sanaimve mix unali usiku atsikana anayamba kumenyana ndipo anamenyana popanda olelesa ndipo atatopelana anangosiyana koma aliyese anali aliwefuwefu

maria za prep zinathela pomwepo anabwelela kwawo kom ak*ti azilowa ku mpanda wa kwawo masautso anatuluka ndi touch ndikumuunika anali odabwa kumuona zovala zimene anavala maria zinali zotuwa apa masa anamufusa chifukwa chimene chadesa zovala koma maria sanadise anafotokoza bwino kwambri za ndeu imene amamenyana ndi Hanah.

apa masautso zinamukhuza kwambri popeza panalibe chifukwa chak*t angathe kumenyana anamupepesa maria.

mawa lake ku school masautso anapita atakwiya ndipo sanafune kukumanaso ndi Hanah pot nthaw ya break ikakwana amapita ku kawelenga.

ataweluka masautso anaganiza zot bola angothesa ubwezi wake ndi hanah popeza anaziwa k*t chikond chawo chitha kuwapasa mavuto ndipo anamulembela message yomuuza Hanah k*ti weekend akumane koma hanah sanakane analola kt azakumana popandaso chophinja.

apa masautso anali osangalala kwambri mix anali akumufuna maria ndiye amaziwa k*ti azakakathesa nd Hanah zizakhala bwino k*t azagwile maria.

weekend itafika maria anamupempha masautso k*ti akupelekeze kwina kwake apa masautso anakopeka kuiwala zoti akufuna akumane ndi hannah ananyamuka ulendo omupelekeza maria koma alimunjila anakumbukila ndpo panali povuta k*ti abwelele koma anangomutumizila hanah message yomuuza k*ti alibizy akumane chama six mazulo.

zinathekadi apa anali osangalala ndipo anayenda mopanda mantha kom akudusa pena pake panali malo okongola ndipo anatenga phone yake ndikumupasa maria k*ti amujambule ma pic koma maliya atailandila phone ija analowa ku inbox kwa hanah ndikulemba mau otiiii.....NEXT

OSAIWALA NDIMAKHALA MA BIZY NDIYE NDINAPELEKA MWAI OTI MUSANTHE NDPO MUNASANKHA MON,WED,FRI.

TIKUNANESO WED...

16/03/2025

TEARS OF LOVE.
PART 1
pangan follow page...
Note:nkhan iyi ndiilemba ngat ma like akwane 45.

yes dailing mwabwelako kale ku ntchito koma ndiye mwapanga changu bwanj kapena mukudwala.

kod mafuso onsewo bwanj osandipasa mazi okumwa kaye ndiye uzindifusa mafuso opepela akowo.

pepani amuna anga koma sinanga ndikudabwa k*ti zitheka bwanji kubwela nthawi zino ku ntchito.

Ruth zoona ukukanika kukanditengela madz

mmm ndinaiwala basi ndikak*tengeleni

ili linali banja la aphiri limene linali banja la new linali lisanathe nyez chibalisilen abusa

ruth...koma ndiye ndikumakusowan

kundisowa kwake kwa mtundu wanji.

chikond chanu ndikuchisowa kwambri koma ndikuziwa k*ti mukumakhala bizy ku ntchto kwanuko koma weekend tizipasanako mpta k*t tizicheza ngat banja la new osamangokhalila pa phone.

waonatu ukuyambaso nkhan ina kod mesa iweso uli ndi phone bwanji tizingocheza pa phone pomwepo.

mmmm anthu tili awiri wiri muno ndiye mpka tizionenga bundle kumacheza pa phone.

ndikhalile chete ndi nkhan zakozo eko ndalam iyi ukandigulile zipaso ndidye

Ruth atangochoka mike anazalandila message yachilendo mu phone mwake koma atamufusa munthu uja k*ti ndi ndani sanachedwe kumudziwa.

uyu anali bertha chibwez chake chaku school ya ukachenjede anthu amalonjezana k*ti azakwatilana koma atangosekela anasiya kulumikizana koma zinatengela bertha kupeza numbr ya mike kuzela kwa ma best friend a mike.

bertha anamufuna Za nkhan yawo imene amalonjezana ku school apa mike anamunamiza k*ti sanapeze mkaz ndipo bertha zinamisangalasa kwambri mix mike amamukonda kwambri komaso amafuna atazamukwatila ndiye atamva k*ti alibe mkaz anazitenga ngati ndi mwayi waukulu k*ti akumane ndik*ti azacheze koma atamufusa za malo okumanilana mike anamuuza k*t azamupeza kunyumba kwake kumene akukhala.

komaso zinamukwenya mabanja atamuuza k*ti akufuna azakhaleko mwina kwa week imozi k*t azacheze bwino.

apa mike mutu unayamba kuwila kena amaona ngat bola kungomumasukila ndikumuuza chilungamo koma akaganiza ndi body limene anali nalo bertha zimamuwawa k*t anapanga phuma kwambri kukwatila Ruth koma sik*t amazilesa kwambri chifukwa chinalipo chokwanila ruth analiso tsikana amene anapanga naye ubwez ali primary komaso ndi munthu oti anachosana unanyali ndiye anaganiza za bertha analiso mkaz anamuchosa unamwali apa mutu unakula mike simasewela

Ruth atachoka k**ika anayamba kumukomzela chakudya mike koma mike sik*ti anasiya kuchexa nd bertha analibe macheza akupitilila amangomwetulila pa phone ruth anali akuona k*ti mamuna wake wakondwa pa phone koma analibe mpata okamuyandikila kapena kuona nawo pa phone mix analiso akuphika.

atamaliza kuphika anakaika chakudya pa table ndikumuuza mike k*ti akadye kom akudya phone ya mike inaitana ndipo mike anaiyankha koma anadabwa akumuonapo bertha apa ndipamene anasiya nsima k*thamangila panja k*ti akayankhe phone komaso amapangila k*ti ruth asaziwe k*ti akuyankhula ndi ndan atatuluka nyumba muja ruth anadabwa mpka nayeso anamusata atangotuluka anamuonaso mike akusunthapo pamalo anakhala paja......NEXT

IKANGOKWANA MA LIKE 45 izibwela ina nthaw yomweyo.

14/03/2025

💔CHIKOND SAYESANA💔
part 2.
pangan follow page.
masautso anali odabwa atamuona happiness akukisana ndi nyamata wa chamba wina amene amantchuka ndi makhalide oipa apa sanazitengele anakangodusapo ndipo anali ndi nkhawa mix happiness anali best friend wa hanah ndiye amangoganiza k*ti hanah so amapanga zomwezo.

hanah atafika ku school anali odabwa ndi mene amaonekela masautso ndipo anapita pafupi kukacheza naye k*t aziwe zimene zamupangisa azioneka zina zake.

masautso anakanika kumasuna mix amafuna k*t hanah asaziwes za nkhan imene ndipo anangokhala chete potengelaso k*ti amamukaikila ndi kale ndiye anaziwa k*ti akangomuuza ikhala mbola .

Hanah sanalimbane nazo anangochoka kukakhala pa Desk ya happiness ndik*tamba kucheza.

happiness zik*theka koma lero wabwela fast mPak kundiposa ine.

mmmm mesa ndinafulumila ndimafuna ndikakumane nd mada chibwez changa chija komaso ndimafuna ndikamupemphe ya ku salut mix ukuona mutu mwangamu ndakhalisa osamanga mesh ina.

uli bho bwanj ine kaya angandilole masautso k*ti andigaile ndalama

atha kulola iwe koditu amene uja ndiwako kapena ukufuna umusiye k*k koma ndiye kungomusiya ine ndipita ndikayese mwayi.

zimenezo ayi kod ukufuna chilichose chizikhala chako mesa uli nd boyfriend kale iwe.

asanamalize kucheza munatulukila sir amene anayamba kuphuzitsa maths ndipo atamaliza munalowaso madam amene anaphuzitsa Bio kenako anapanga break.

apa ndipamene masautso anamupasa zakudya zimene anatumidwa ndi hanah k*ti amutengele.

Hanah anangoyamika ndipakamwa pokha ndikumapita izi zinamuwawa kwambri masautso mix amafunaso hug koma anangozisiya basi iweyu ndikumalemba notes zake ali pheeee.

akulemba notes zija kunabwela maria amene anali neba ku nyumba kwawo ndipo anakhala pa Desk paja ndikuyamba kucheza ndi masautso.

kodi masa iweyo zikuk*thekela

kwambri ase koma pena zikukanika

bwanji...

mmm zimene ndikuziona ine pa hann...

asanamalize anandizidula mix samafuna k*ti maria aziye k*t ali nd girlfriend apa anangoipitisila kwina.

koma ukuoneka oti ukudisa china chake ndimasukile ase.

apa masautso anamuyang'ana kumaso ndipo mmm anadalalika kwambri mix maria so anali ka tsikana kokongola wez.

mmm basi ase ukuziwa kale ma relationship amasiku ano mene amayendela munthu umangokhalila kunkhumudwa.

maria zinamudabwisa kwambri yankho anapeleka masautso ndipo anafuna k*ti amve zambri koma belu lolowela chinalila.

anangochoka kukakhala pa Desk yake ndipo anali nd zimafuso zambri kwambri.
anaphuzila ndipo ataweluka

Hanah anafuna k*ti ayendele limodz popita kwawo ngat mene amayendela ma guyz azawo amene amayenda ali pa ubwez pa school po

koma zachisoni anamuona masautso akuyenda nd maria izi zinamunyasa mpka anatola mwala k*ti amugende maria koma china chake chinamupeza basi anangosiya mwala uja ndikumapita koma amaoneka okwiya kwambri anayenda mpka kukawadusa.

masautso anaziwa k*t talakwa koma sanazitengele mix amamukaikil kale atafika kwawo anapeza message mu phone mwake yolembedwe k*ti.

Ndili ndi msanje kwambri nditamva zoti uli nd chibwez kod sungayeseko kwaine

message imeney inali yodabwisa kwa masautso mix number inali yachilendo koma atamufusa munthu uja sanayankhe k*t Dzina lake ndi ndani koma anangomuuza k*ti azamuziwa ekha k*t anali ndani.

masautso anadya chakudya chake chamasana ndikulowa ku room kwake kuyamba kuwelenga ndipo tsiku ili sanakwanise kuwelenga mix ndima message aja amamudalalitsa mutu koma anangoti basi tsiku ndili modz azamuziwa munthu amene akupanga zimenezo.

atatuluka ku mpanda anakumana ndi maria nayeso anali akungotukul ka ku mpnda apa onse anangofikila kusekelelana mix ma zinebaz.

masautso anamupelekela maria ku mtsika ndipo ali munjila anamasuka ndikuyamba kumufotokozela zama ma message amene amarumizilidwa aja koma maria anangoti okay.osatulusa mau ena mayankhidwe awa anamupasa mafuso masautso.

atafika ku msika masautso anapita pamene panaima car ya kwawo ndipo anamupeza driver ndikumuuza k*ti amupaseko ka 5pin ndipo driver uja anapeleka.

apa masautso anatengana ndi maria k*t akadya chips koma atagula ndikulowa modyela chips masautso anagwila kukamwa anaona........NEXT

NDIMENE ZIKUKHALILA PAJA MUNASANKHA MONDAY..WEDNESSDAY...FRIDAY...

NDIYE ZIKUONESA K*T ANTHU SIMUKUIPASA MOTO SIICHEDWA K*THA

TIONANE MONDAY....

12/03/2025

💔CHIKOND SAYESANA💔
part 1...
pangan follow page.
osaiwala kupekaso like komaso comment.

Hanah plz ndipaseko chikond choonadi ine pano.

kod ukufuna chikond chamtundu wanji masautso ndiuze ine sindikukwanisa pat.

wafusa fuso labwino ineyo ndikufuna pena tiziyendela limoz k*ti ma boiz amzanga aziziwa k*ti ndili nd girlfriend kumanena iweyo.

okay ndakumva koma sik*t uzichita kundikakamiza mapeto ake ndithesa chibwez chi kaya tamvanapo apa.

uku kunali kucheza kwa masautso nd chibwez chake morin.anthuwa chibwex chawo chinayamba mosavuta anangocheza kwa ma dayz ochepa basi masautso kugwesela mfunda kwa morin nayeso morin anangolola k*ti basi akusangalase masautso.

atamaliza kucheza kwawo anasazikana ndikunyamuka kumapita wina aliyese kwawo.

koma morin akuyenda anakumana nd mzake amene ali happiness ndipo morin anamumasukila mzake uja ndikuyamba kucheza naye

ase happiness ine zachikondizi simbali yanga mmmm ai

bwanji ase pali pamene pavuta nd masa uja

ndikungoona ngat ndinaziyamba ndisana nkhwime mzeru.

mmmm ase uzitolele iwe sukuziwa k*ti amene uja utha kumangomudyela nanuso tachenjelan morin.mwait subwela kawiri.

mwai subwela kawiri ndiye uk*tanthauza chani ase.

ndikuuze kodi mesa masautso uja kwawo kuli sienta ndiye iwe uzingomudyela ndalama mesa iweso ukupusatu ndikulanda chifukwa ine sindimasewelesa mwai.

apo ndiye ukunenadi zoona ase ndikuyenela ndisaumphonye mwai umenewu ndithu ndiye uzindithandiza ma skill eti

usaope ase ine ndine acter pazimenezo upange zoti ku school tisamasowe ndalama yodyela zigege.

atacheza anasiyana mix happiness anali atatumidwa kwao k*ti akagule ndiwo zamazulo

morin atasiyana ndi happiness anayamba kuganiza za zimene amamuuza mzake zija koma pena amazitenga ngat ndizosagwila koma akangokumbukila nkhan ya ndalama pompo amalimba mtima.

anayenda atafika kwawo mai ake anamufusa k*ti amachedwa k*ti koma iwey sanayankhe chilungamo anangonama k*ti amachedwa kwa mzake happiness.

masautso atakhala kwawo analandila message yochokela kwa morin yoti.

hy be ndimakundonda kwambri mawa unditengele kenakake sinanga ku school kuja njala ikumawawa ndiye nanga ine ndizivutika iwe ulipo siikugwila ineyo plz

masautso ataona message ija anali odabwa k*ti izi anamulembela anali morin koma anangozisiya ndikupita kwa madala ake kukapempha ndalama k*t akadye mawa lake ku school pamozi ndi morin.

anagona ndipo mamawa analawilila kuzuka anapeza zokudya zaphikidwa komaso panali foodomer pa table zimene zindmudabwisa masautso mpka anamuitana wa ntchito kumufusa k*t foodomer muli chani.....

ndipo wa ntchito uja anamunong'oneza kukhutu

mpka masautso anali odabwa k*t waziwa bwanji za nkhan yoti akuiziwa bwanji....

wa ntchito wakwa masautso amachezaso nd happiness ndikumene anamuuza za ubale wa masautso ndi morin.

masautso ananyamula zakudya zija kumapita ku school koma ali mu njila anamuona munthu aku kissidwa.....NEXT

SORRY KAYA IZIBWELA MA PART AAFUPI ZIWAN K*TI NDIMAKHALA BIZY.

YAYAMBA BWANJ.

TIONANE FRIDAY

05/03/2025

CHIZIWITSO.

ma vote athu ma letters amene ndinaika yawina ndiC

ndiye k*t nkhan izibwela monday,wednessday and friday.

mosachedwesana lero ndikuyamba nkhan

TITLED::💔CHIKOND SAYESANA💔

ndiye osamandifusa k*ti nkhan ikuchedwa chifukwa chan ndinalongosola kale k*ti ndimakhala bizy mkat mwa week ndiye apa ndizikwanisa ma day mwasankhawa

weekend mwina ndiziponya ndikasangalala mix ndimakhala free kwambri sartuday ndiye osadabwa ndikaponya weekend.

Ndikufunaso malike ndi macomment azichuluka k*ti ndizibwelesa osadumphiza ma days mwasakhawa.

Zikomo.

TIONANE NTHAW 4:00 LERO

02/03/2025

ANNOUNCE....
Pakatipa ndinazowa koma sindinabwele poyela ndikufotokoza vuto lake eti lero ndikuuzen vuto lake silambili ayi choyamba nkhan ija imene ndinayamba kulemba ija zinapezeka kt app imene ndimalembela nkhan imangosowesa ma part ena ndiye zinandibhowa kwambri ndiye ndinangopuma k*ti bas mutu uzizile kaye.

apapa ndikufuna tisankhe ma Tsku amene ndiziponyela nkhan chifukwa nthaw zambri ndimakhala bizy mkat mwa week.

A..monday,Tuesday,wednessday
B.friday,sartudya,sunday
C.monday,wednessday,friday
D.sunday,Teusday,Thurday.

Mukasankha ndipamene nditabwele ndi mutu wina wa nkhan koma ndizizaponya pa ma day amene mutasankhewo komaso amene amasogolole nd ma vote..

TIONANE TSIKU LOZAULUSA MA VOTE...

10/02/2025

Amene mukungofikila kuwelenga part two ziwani k*t part three ili pasi pa part two....zulo nditamaliza kulemba part two ndinaiwala ku save ndeee yasowa..ndangopanga k*t mumve za mu part two

10/02/2025

MIMBA SI YANGA
PART 2
Mungomva mene zinakhalila mu part 2.

pamene peter amamukakamiza emmie anamugwila mabele ndik*topa.

kenako ananyamuka ndikukumana ndi lirian tsikana amene anali ndi msanje pa ubwez wa peter nd emmie

lirian anamunamiza zambiri peter za emmie kumunamiza k*ti emmie amapanga chibwez nd sir ake amaths k*tengela ndi makhozedwe a emmie maths peter mpka anakhulupilira.

tsiku losatila peter akudusa pa staff room anamva mau a emmie akucheza nd sir amaths.kenako atafika class anakakhala pa desk yake koma ali nd mkwiyo kwambir

koma atangolowa emmie class anafikila kukamukissa peter

apa ndipamene ndinayambila part threee

pepan pepan pepan ndikuziwa k*ti simunakondwe nd zimenezi koma ndikulonjexa k*ti lero kudyaso part 4

5:00pm

plz ndikhululukilen ineso ndi munthu ndimalakwisa

10/02/2025

𝙼𝙸𝙼𝙱𝙰 𝚂𝙸 𝚈𝙰𝙽𝙶𝙰.
𝙿𝚊𝚛𝚝 3
pangan follow page
NOTE.PEPANI PART 2 iibwela ndiye osadandaula part 2 sindinaipange save pamene ndimalemba zulo.
peter amangomva kukoma zak*t amufuse za sir xija anaiwala mpka inakwana nthaw yolowela class ndiye subject yoyamba inali maths omweo sir aja atangolowa ndipamene peter amakumbukila za emmie apa analephela kugela bhbh mix anali nd maganizo oipa kwa sir aja.

Itatha period yawo anakhuka kukafika pa Desk la emmie k*ti akaonedi ngat maths amachita kukopela koma analiodabwa k*ti emmie amalemba ekha maths onse mpka kumaliza apa peter naye anali asakuziwapo kanthu pa maths aja mix anali akuyandiza zina nthaw imene amaphuzitsa ija anangotenga kope la emmie ndikungokopela basi ndikukakhala pa desk yake.

atangokhala wez panatulukila Lirian.

lirian...yes zabhbh

peter....bhbh ase kod wabwela ine sindinakuone mene umalowa class lero.

lirian ....mungatione mukucheza nd akaz azathu kodi.

peter...wati akazi amzako mmmm koma ukufuma ndiyankhule zosakhala bwino k*ti uzitole pakamwa chan.

lirian mene amayankhula peter anali akulemba ka flower pa mwendo wake apa peter amachita kuona ntchafu yonse ili panda mpaka anakhumbila ndikugwila pang'ono chabe kenako k*thawisa mkono wake awa anali matha mix lirian sanali chibwez chake.

koma akanaziwa apa lirian anamugwila peter mkono ndikuika pa ntchafu pake apa k*ti class munalibe aphuzisi ndiye wina ali yese anali akucheza naye emmie amacheza ndi mzake amene amakhala naye.

zak*ti pa Desk pa peter pali Lirian samaziwa anachita kuuzidwa nd mzake koma sanazitengele.

tionge...Emmie koma wamuona mene akuchezela peter nd lirian.

Emmie...Mmm palibe chimene akupanga amene aja wamuiwala lirian amangokonda kucheza nd wina aliyese.

Tionge....koma sukuonapo vutoz ayi mmm koma anthu enawa akazakulanda ndipamene uzagwile mawu anga.

Emmie...zisiye zimenezo Tio

apa anapitiliza kucheza nkhan zina ndipo mpaka class kunalowa ma phudzis ena ndikuyamba ku gelesa mpka nthw ya break inakwana.

Emmie anamusaka peter koma sanamuone apa anangozisiya ndikukakhala class mwawo ndikumasova maths.

peter anali nd lirian kuseli kwa class yayo yochepe kumacheza.

lirian...kod ukundiyang'ana ndatani kodi.

peter...mesa ukhale bwino mmm ine mpka ndizichita kuona zovala za mkat yatani kod

Lirian....kod mesa tikuCheza basi ngat unaona k*ti sindinakhale bwino ukanangonena bsi osayankhula ngat unandiuzapo koyamba ine ndikukana ayi.

peter...sorry koma ndingafuseko.

Lirian....kufusa chan peter.

peter.....ndimafuna ngat kuli kotheka tiyambe kupanga chamseli.

Lirian...mwamseli zichan

peter....ndikufuna ukhale chibwez changa koma emmie asamaziwe.

Lirian....zimenezo ndizosavuta koma ndikaganize kaye chifukwa pena ndikuopa kwambri.

Peter...kuopa chan liri.

Lirian....paja amat njoka yofasa imalumila ku mchila emmie kungoziwa ndili madz.

peter...aziwa bwanji kod mesa amakhala kwawo iweso kwanu ineso kwathu toseso tili nd maphone..

belu linalira apa anangosiya aliyese kumapita kumene amafusa pa nthaw.

lirian anali ndimantha akulowa class ndi mene amamuyang'anila emmie apa anaziwa k*ti emmie wamukaikila china chake.

TIAZIWE ANTHUWA

LIRIAN anali ndi mzaka 17 amachokela kubanja lochita bwino.

peter anali ndi mzaka 19 nayeso amachokela ku banja lochita bwino wez.

Emmie anali nd mzaka 17 amachokela ku banja lolemela kwambri mu dela lonselo.Cont...

peter atalowa class anafikila kulemba ka note ndikuponyela Emmie kalembedwa mau oti

"""anandiitana sir a eng ndiye ngat sunandione ndinali kumeneko""""

emmie atawelenga anangomuyang'ana peter kenako ndikung'amba ka note kaja.

anaphizila mpka kuweluka emmie ali mu njila anakumana ndi Tionge.

Tionge...ndamuona peter ali nd lirian

emmie...mmm zisiye zimenezo.

Tionge.. tamuone uja akuchita kugwilana gwilana.

Emmie anayang'anako akaonadi k*ti ndizoona apa anayamba kuyenda mwa fast ndikukafikila kumugwila Lirian pakhosi....

09/02/2025

𝐒𝐢𝐤𝐮𝐭𝐢 𝐩𝐚𝐫𝐭 2 𝐬𝐢𝐧𝐝𝐢𝐧𝐚𝐥𝐞𝐦𝐛𝐞 𝐢𝐥𝐢𝐩𝐨 𝐤𝐨𝐦𝐚 𝐧𝐝𝐢𝐦𝐚𝐟𝐮𝐧𝐚 𝐧𝐝𝐢𝐨𝐧𝐞 𝐤𝐮𝐭𝐢 𝐦𝐰𝐚𝐢𝐥𝐚𝐧𝐝𝐢𝐥𝐚 𝐛𝐰𝐚𝐧𝐣 𝐤𝐨𝐦𝐚 𝐳𝐢𝐤𝐮𝐨𝐧𝐞𝐬𝐚 𝐤𝐮𝐭 𝐦𝐰𝐚𝐢𝐥𝐚𝐧𝐝𝐢 𝐦𝐰𝐚𝐮𝐥𝐞𝐬𝐢 𝐧𝐝𝐢𝐲𝐞 𝐢𝐧𝐞𝐬𝐨 𝐧𝐝𝐢𝐳𝐢𝐤𝐡𝐚𝐥𝐚 𝐧𝐝 𝐮𝐥𝐞𝐬𝐢 𝐨𝐩𝐨𝐧𝐲𝐚 𝐭𝐢𝐨𝐧𝐚𝐧𝐞 𝐦𝐚𝐰𝐚....

𝐓𝐎 7.....

𝙼𝙸𝙼𝙱𝙰 𝚂𝙸 𝚈𝙰𝙽𝙶𝙰.𝙿𝚊𝚛𝚝 1.pangan follow page.Note:izibwela daily ngat ndikulandila mulalo ochuluk kumalike komaso ma comment...
08/02/2025

𝙼𝙸𝙼𝙱𝙰 𝚂𝙸 𝚈𝙰𝙽𝙶𝙰.
𝙿𝚊𝚛𝚝 1.
pangan follow page.
Note:izibwela daily ngat ndikulandila mulalo ochuluk kumalike komaso ma comment...

Emmie koma iweyo sumapanga bwino ndithu nthaw zambari umangoti uli bizy olo ma weekend sitimakhala ndimpata ocheza malo amodz.chimenech ndi chibwez kapena macheza.

uyu anali peter kumufusa emmie amene anali chibwez chake.

Emmie...ndikuziwa k*t ndimalakwisa koma iweso ukanangoyenela kundimvesesa mix kwathu kuja ndikovuta samandilola kuyenda nthaw zambri ndiye ine nditani kd mesa timacheza pa phone.

peter...ndikuziwa k*t amakukaniza koma iwey uzipeza plan yochokela kwanuko mesa kwa neba kwanu kuja kuli tsikana utha kumanama k*ti ukupita kumeneko ukubwela kuzakumana ndiineyo mesa.

Emmie....imene ndiye mbola peter masten anga amapita kumene kuja kukacheza ndiye nditanama k*ti ndikupita kumeneko zingandithele bwanj ineyo.

peter...okay pasa vute nthaw imene azik*tuma ku msika tizikakumana komweko kaya kumacheza wez ku logi basi ukuona bwanji.

Emmie....mmm mpka ku logi koma uli nazo srs yeti ndiye ndikachedwa kukafika ku nyumba mesa azikandikalipira.

peter....mmmm kukukalipirako ukadandaule mesa amakalipila basi ndik*tha plz ndimveseko kukoma penapake ineso ndimalifuna thup lakolo emmie.

Emmie anangovomela k*ti azione mene azikumanilana kenako anasazikana emmie kumalowa ku mpanda wakwawo.

apa anali akuchokela ku school atalowa kwawo anafikila kudya ndikuyamba kuwelenga notes.akuwelenga chochija analandila message yoti.

emmie bwela ndili panja pa mpanda ndabwela pa njinga ndizak*tenge tikacheze wez.

ataiona message ija anali ndi mantha k*ti akatuluka bwanj pa sitting room sakamufusa mafuso.anazayankha message ija.

peter ndikuopa makolo anga abwela kale ku ntchito sindingatuluke andikalipira.

peter ataiona message ija zimunyasa nayeso analemba yake.

okay chabwino ndapita koma ukazamva zoti ndapeza chibwez china osazalira tamvana kaya ine ndatopa nazo zimene tizingocheza k school kokha.

emmie atawelenga message ija analiziwa k*ti peter wakwiya ndipo athadi kunyamuka apa analembaso yake.

basi ndikubwela koma nditulukila pa windol pa get so sindikwanisa kudusa chifukwa amva kulira kwa get ndikamatuluka ndiye ubwele kuseli kwa mpanda k*t uzandigwile ndikamatuluka.

apa peter anasangalala pamenepa chifukwa anaziwilatu k*ti apa pokha akachezako ndi bwez lake emmie kwa nthawi yoyamba.

anathamanga ndikukafika kuseli kwa mpnda kuja ndikumulembela text kumuuza k*t atha k*tuluka.

Emmie anatuluka mwakachete chete mpaka anafika panja pa mpanda anangofikila kuhagana apa peter sanangomusiya koma kupotiliza mpka kiss kenako anamwamuka kumapita pa njinga.

anayenda mpaka anakafika mbali mwa nyanja ndikukhala kuyamba kucheza.

peter...apa siwaona watuluka ndiye umaopa chan basi apopo uzingotulukila pomwepaja.

Emmie...kom ndinali ndimantha wamva mmm komaso zotulukila pamene paja sindingapange kwa neba kuja kuli agalu ndiye siku lina atha kunzandikuwa mapeto ake ndikundigwila.

Peter...okay koma nditamalowa inepangakhale povuta eti.

Emmie....mmm ai bola iweyo uzilowadi koma ine k*tuluka ndimbola iweyoso ndiye k*ti nditha kumakakiya pa khomo ndiye k*ti akamakagogoda utha kumakalowa k**i kwabed.

peter...ukuiwala k*ti kul ka ccta kako kaja ka faith.

Emmie....amene uja akangodya amapita kosewelela ndiye ndimasala ndekha.

peter...okay bhobho ndiye tasendela kunotu ndigwila nawo.

apa peter anali atayamba kale kusewelesa mabele a Emmie.amachita kumafinya bwino.

Emmie.....mmmm peter zimenezo sizabwinotu zoona uzindigwilaso mabele.ndisiye tiye tizingocheza.

peter sanasiye kugwila mabele aja anagwila mpka pamene anatopela.atamaliza anamuuza k*ti asambe limoz.

Emmie...mmmm zosambazo ayi basi bola ndizipita kwathu.wandigwila mabele apa uk*t ndivule tikasambe sindikwanisa ine.

peter....plz ndi lero lokha chabwino

Emmie....bola tsiku lina lero ndakana ine.

peter anangozisiya koma zinali zikumuwawa mumtima mix anafunisisa k*ti atasamba limoz ndi emmie anakhumudwa koma sanafune kuzionesela.

ananyamuka kumapita apa anayenda mwa fast kwambiri mpka kukafika pamene anatulukila emmie.

anasika njinga ija apa peter anangofikila kulowesa mkono wake mkat mwa mabele a Emmie.

Emmie anazizimuka wagwidwa kale bele.

Emmie...ndisiye peter ndikulowe kod mesa tacheza apaso ukufuna uzitaniso undigwileso mabele.

peter....ngat sindigwila ndiye k*ti sindikukweza pa mpanda ndiye k*ti makolo ako aziwa k*ti unatuluka.odi ndizipita.

akunyamuka Emmie anamugwila mkono kumulesa k*ti asapite....... 𝙽𝙴𝚇𝚃

𝙸𝚈𝙸𝚂𝙾 𝙽𝙳𝙸𝚈𝙴 𝚈𝙰𝙽𝙶𝙾𝚈𝙰𝙼𝙱𝙰 𝙼𝚆𝙰 𝚄𝙺𝙰𝙻𝙸 𝙱𝚆𝙰𝙽𝙹

𝘺𝘢𝘺𝘢𝘮𝘣𝘢 𝘣𝘸𝘪𝘯𝘰 𝘪𝘱𝘪𝘵𝘪𝘭𝘪𝘭𝘦 𝘯𝘥𝘪𝘱𝘢𝘴𝘦𝘯𝘪 𝘮𝘢 𝘤𝘰𝘮𝘮𝘦𝘯𝘵 𝘢𝘱𝘰𝘸𝘦𝘳 𝘬𝘶𝘵𝘪 𝘯𝘥𝘪𝘻𝘪𝘺𝘦 𝘯𝘨𝘢𝘵 𝘺𝘢𝘬𝘶𝘴𝘢𝘯𝘨𝘢𝘭𝘢𝘴𝘢𝘯𝘪.

𝘛𝘐𝘖𝘕𝘈𝘕𝘌 𝘕𝘛𝘏𝘈𝘞 𝘐𝘕𝘈𝘈𝘈𝘈

Address

Tam
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Spim vallihar posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category