Bwalo lamacheza

Bwalo lamacheza Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Bwalo lamacheza, Grocers, Blantyre.

05/03/2022

Zimangoona kuvuta koma nkazi winaaliyese amakhala ndi thako

05/03/2022

Uziyamba waziona Kaye ukamanyada wava mwana ubadwila patchilewe

25/02/2022

Wanuyo sakumufu chifukwa----------???

22/02/2022

kod asing'anga mumakanika kupanga post Khan yanu why mwina simunapite ku xool et nde lekani zopusa zanuzo πŸ‘Œ

22/02/2022

mukakhaka m'banja mwanumo mukayambana musamatiuze ife coz mene mumakwatilan ife panalibe nde be careful

14/02/2022

Valentine imeneyi Elli njuchi zikumuthela Bwanji pomwe mahop ake ali NdIwinaπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

14/02/2022

Chomwe chandinyasa relo k*tsegula πŸ“» k*t ndivele khani ndangova baby ukandikodola kodo kodo eeeee ufulu πŸ“» ndi dj Jerald kanyama wandibowa πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ“» station πŸ“΄

14/02/2022

Ndikumusakasaka koma sindikumupeza kupitakwawo dzulo osampeza chonde mumuuze Swazi zangauja yemweanakanidwa ndi saingie uja kt lero zitivutaπŸ“΄πŸ”₯πŸ’₯πŸ‘

13/02/2022

usayelekeze kunena zapa 14th February tiyambanapo Swazi sapanga nawo nyasi zanuzo
,
Dzai mw

Address

Blantyre
COMEDY

Telephone

+265883253920

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bwalo lamacheza posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Bwalo lamacheza:

Share

Category