Macheza akhani zachikondizi

Macheza akhani zachikondizi Ndinagwa chikondi zaka zochuluka kwabasi ndiye zinazi zikamachitika ndimangoyangana poti sakundiwa ay

11/03/2025

Hy amalawi

22/02/2023
16/01/2023

Khani yanga title timakumana bwanji two ilipo page yomweyino

12/01/2023

Tinakumana bwanji part 2

Joanne ananyamuka pamalo panja komaso Judith amaseka mwachinunu Joanne atafika kwawo anangolowa nyumba kumagona Sono Judith anafika kwawo kuyamba kuzifusa ekha akuti akundifuna ine komano ndizanga kuyambila kalekale ndiye ndizichitila manyazi kwambiri pazithu dzina kenaka Judith anaganiza zomupasa mayesero Joanne *tsiku litakwana laku school Joanne atamuwona Judith anamuthawa kukalowa class ndipo Judith anawuza azake kuti akamuwuze Joanne kuti Judith alindi chibwezi izi zinachitika komano Joanne anasiya kucheza naye Judith cholinga chenicheni sanachipeze after one week Judith anamulembela kalata yomuyitanila kwawo Vuto linalipo ndilokuti mayi ake a Joanne akagwila ntchito kwa Judith komano onsewa samaziwa.mawa watsiku lachisanu tsiku lomwe Joanne akapita kwa Judith dzinali zooopsatu azanga atangolowa anapeza mphokoso akukangana Judith ndiwantchito wakwawo amane alimayi ake a Joanne atayandkila kuwawona amayi ake and Judith akutukwana mayi ake kungowona mwana??kuwona mayi?? Maso mwawo misozi

Osayiwala kupanga like and follow my page ndikunena next ngati yakusangasani ngatiso palivuto ndiuzeni ku ibox

11/01/2023

Tinakumana bwani part 1

Dzina langa ndi Joanne ndimaphuzira pa school yochedwa mlakati ndinali form one ndinzanga yemwe dzina lake ndi Judith.. Judith wakhala zanga kuchokera ku primary yathu Koma olo anali zanga ine ndimakonda 💕 ngati chibwezi changa komano Vuto ndinali ndi matha kuchokera kwawo kunali kwandalama kwambiri and winawake anandiuza kuti ndimaoneka kuti ndimakonda Judith koma ndinali sanamuwuze kunenesa linakwqna thawi yomww ndimaganiza zomuwuza ndipo dzinali chochi.
🦓 Koma Judith ndilindi mawu
🦄mawu anji naweso apa
🦓ndikubisa mawu kamwa kulakhula mofuna kuwina mlantho oloka mtima wako ndiye Pali khope yakanzi ndi pillow wanga amene ndingafanize kuyandikana ndimtima wako kwaine
🦄 ukukamba ziti koma Joanne.
🦓ndilikozeka kuyamba kusaka zokonda zako ndikuwuza ukabwera mutima mwanga ukhala queen bed wanga
🦄Koma ndizoopsa kwaine chifukwa sinakondepo ine komano
🦓 ndinkhoza kukwanisa kukonda Koma ngati sunandikonde ukandiona mumtima mwako ndilimomo Koma ndilindi njara yachikondi ndiwe
🦄ndizovuta kwaine siwe mamuna kwa amuna

Izi zinandipasa ndikhawa kuti akukamba ziti makamaka Joanne anangozuka kuyamba kulila uku akuthawa mpompo Judith anayamba kutseka mosazionesera

Ndiuzeni%ilibho kapena ayi komano ngati ilibho ingombani next Basi don't forget to follow up my page and like

28/12/2022

Chooooooooooooooooooooooopooooooooooooooooooooooooooopooooooooooooooooooopooooooooooooooooooooooooooooooonde help me adim ndithandizeni kugawa khaniyi

Dzulo ndinangowona chibwezi changa akubwera kwanthu atangofika mwachizowezi ndinapasa milomo kenaka anazakhala ine ndinafusa mfuso ndivekere bwanji ukuwoneka sunasambe anayamba kulila kundikhumbatila uku akulilabe kufusa avekere kwanthu anapeza ma picture ako ndiye andimenya kwambiri zoti ndatupa kwambiri ndipo anavula kuona mene amenyera mayi ake pamodzi ndibambo ake ine monga ndinatothoza ndinu kupanga zoti asambe alongosole zonse zachitika anandiuza kuti bamboo amene amakhala nawo ndiwo opeza sibambo ake enieni ayi ndiye amamuda kwambiriso poti anatengerapo mwayi pa issues imeneyi 🌉 anafika time ya chama1 masana paka chama6 ndiye poti chibwezi changa ndinamasuka paka ndinagonana naye titamaliza kugonana anandiuza kuti ndiperekeze kamusiye kwamzake agginess kenaka ine ndinaperekeza ine kumabwerera$$$ mawa kutacha ndazuka ndapanga chilichose chofunika mawa Basi ndati ndikayende guys guys guys guys kanzidi ndifiti ndizoonadi guys:-D:-D ndakumqna ndizake akundiuza Jennifer alikuti ndamuwuza alikwawo Kodi ukufuna akuti ayi ayi ayi mayi ake anabwera kwathu zoti amafuna kwambiri sanagone kwawo ndiye ndimawona ngati kuti wagonatu kwanu zoti nakubisa kuti ndizake chabe sanagone kwawo ndikufusa kuti chachitika chani ngakhale anandiuza kale ndimangofuna kupanga confirm anandiuza kuti anapeza alindi mamuna kuchipinda kwake zoti mayi ake anamumenya kwambiriso moti kulilako amamva ululu kwa akumuthamngisa sindikuziwa ulibwAnji komwe aliko komano usamale ngati wagonana naye no

Ndiye guys ndithandizeni kuti ndipange bwanji nanga wandinamiza zomwe zachitikila komaso ndagonana naye nditani ine guys

Osayiwala kupanga like ndikupanga follow my page please please don't forget to follow my page

27/12/2022

Chibwezi siii banja mwamva

24/12/2022

In This Whole World You Are Just Somebody,
And For Somebody You Are The Whole World.
That Stupid Somebody Is Me.
I Love You Somebody.
Happy Propose Day.

22/12/2022

Zikomo pondipasa 2k likes and comments 1likes💕💕📸 mpunga wanyama basi

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Macheza akhani zachikondizi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category