The truth vomiter

The truth vomiter Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from The truth vomiter, Grocers, Phalombe district, Blantyre.

10/05/2025
Si onse amene muziwatenga ngati anzanu kumasamala ndi enawa Ali ndi ululu wamamba
10/05/2025

Si onse amene muziwatenga ngati anzanu kumasamala ndi enawa Ali ndi ululu wamamba

15/07/2024

Send a message to learn more

15/07/2024

KODI MUKUDZIWA KUTI DZIKO LA MALAWI LILI NDI NGONGOLE YOKWANA 16 TRILLION KWACHA KUCHOKERA KUMA BANK AKUNJA MABUNGWE NDI MABANK ENA AKWATHU KONKUNO?

NGONGOLEI YACHULUKA CHONCHI CHIFUKWA CHANI?
boma likudalira kwambiri katundu wakunja ndipo likukanika kutulutsa katundu kumaiko AKUNJA kuti tipeze forex.

NDIYE BOMA LAGANIZA ZOKWEZA MITENGO YAMAFUTA. NDI ZINTHU ZINA KUTI LIPUNGULE NGONGOLEZI

KOMA2 SECRETARY TO THE TREASURE DR BETCHANI TCHERENI SIKULALATA KWAKE

iwo akuti amalawi mumawaopseza andale kuti tionana pa chisankho ndiye pa chifukwa ichi boma limakanika kupanga zinthu chifukwa cha pressure imene amalawi amawapasa
Ndipo iwonso akuti. Mukaona nduna za boma zikuyendera galimoto zodula za 150 million KWACHA (VLX) mtima wanu uzikhazikika szoti bas zonena kuu! Chifukwa ndi nthawi yao bas kuti asangalale nzosiirana izi
Ndpo iwo apitiriza kuti Kodi mmafuna aziyendera galimoto za 25 years ago ngati si Ali m'boma?

The truth vomiter

Send a message to learn more

Address

Phalombe District
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The truth vomiter posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category