Mr Deeh.

Mr Deeh. This page Is Created to give you True life stories

23/08/2025

This is from Mr Deeh

MWAYI WA GANYO

Guys ineyo ndakazanga tikugulitsa ntchito pa mtengo wa R7500 ine garden boi alazanga nanny ine ndimalandira R9000 alazanga R12000 anthufe tikupita ku muji nde oikonda ntchitiyi nditsatira comets

Interested inbox πŸ“₯ Admin

17/08/2025

This is from Mr Deeh

Job opportunities in Cape Town

Anthu four akufunika mizinda iyi kuli mwai wa ntchito in cape town

Cross roads kukufunika shop atendance kmas maid

Retreat kukufunika garden Boy

Western cape kukufunika cooker

Interested Hit Admin
All the best!!!!

17/08/2025

This is from Mr Deeh

Pali mwai wa ntchito yanyumba kwa munthu wamai ku blue down stay in

Kuli mwana wa 6 months komaso azikagwilaso zina nd zina mnyumba

R5500 per month
Kukufunikira munthu ali nd passport and kwa amene amatha kuyankhura english bwino bwino momvana nd munthu

Interested please Inbox Mr Deeh

17/08/2025

Hello Mr Deeh

Am a man zaka 30 ndili ku South Africa cape town ..mr deeh ndikufuna nkazi yomwe ali ku cape town kuno.

I want a stable relationship ndilibe mwana and not married before koma nkazi atakhala k*ti ali ndi mwana akhale mmodzi basi

Zaka from 24 to 28 ..working or not working..ine am working

If muli interested in him just Hit Mr Deeh

16/08/2025

Hello Mr Deeh, hope you are good. Please help to connect me to someone (blesser) nsaname munthune nduvutika I have been trying to save to start a business but mmmmm always comes up as I am saying ndili pa zero am a single mom as of today I don't know what I will feed my baby, I stay in Mangochi. Thank you

16/08/2025

Hello Mr Deeh!

Ndilemba mu Chichewa aliyense andivere.
Ndine mzibambo wa dzaka 30 ndimakhala ku Blantyre sinakwatilepo.
Anthu ndiweluzeni koma zabwino zonse ndalepheraπŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ™Œ Me Deeh ngati muli ndi mzimayi woti akufuna kugonedwa ndi mwamuna ndipangeni connect Mr Deeh ndiri ndi ngongole ine MK650000 thousand kwa anthu wosiyana siyana onse ak*ti akuzifuna ndalama zawo pa 30 mwenzi uno. Ndasaka maganyu ndalephera πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ™Œ ntchito kumene zandivuta panopa ndikumaganiza bola kufa nanga ngongole za anthu adzabweze ndani. Or ngati pali azibambo woti atha kundibweleka ndalama yo ndek*ti Chikole atenga ma Certificate anga onse singathawe ineyo ndathedwa nzeru mutu sizikuyenda chonde anthu inu πŸ™πŸ™πŸ™ thandizeni abale ndisafe ndi stress.
Business yanga inatha December pomwe Galimoto yomwe inanyamula tomato πŸ… wathu inagwera ku tchire chiyambi cha mavuto anga chinayambira pamenepo.

Ndiribe phone ndabwereka. Aliyense wolumikizana nane adzere kwainyo Mr Deeh 😭😭 nzeru zandithera msaname.

25/07/2025

This is from Mr Deeh



kuli ntchito ya sleep inn, (Cleaning & cooking) location Rasternberg , Salary 4000 munthu akufunika wkeed k*tuluka kawiri pamwezi,

Interested inbox Admin

24/07/2025

Pali Zibambo akufuna mtsikana zaka Malire 25 Akhale opanda Mwana, Akhale Ooneka bwino wa Hit and Run Ali ndi 150k Akhale wa around BT Machinga Zomba or around this District akapezeka inbox me

25/04/2025

This is Mr Deeh

Choyamba basi ndaseka ofuna thandizo

Chachiwiri muthu uyu akufuna omwe akusoweka chakudya

Mavuto azingongole apa sakulowa or a business

Mwini wake yomwe akufu kudalutsa akufuna omwe akusoweka chakudya ndipo aziwayendera komwe ali anthuwo

Budget yanga ndiya 2 Million koma ndimafuna ifikire anthu 20 k*t aliyese azilandila 100pin.

Awiri alipo kalewo ndi ena 18 koma sindikuziwa zot Tingawapeze bwanji pa page yanuyi monga mwakambira k*t Pandalama pali payesero koma ndili sure k*t Nditha kuwayendera makomo mwao komaso nditha kumawafusa mafuso omwe ineyo nditha kuzindikira k*t munthuyo ndi ovutikad kapena ayi

May God people like him...you make this page a place to be when in need.

I have closed k*tenga anthu

Tikamanena k*ti don't take everything Tomaida Saka amanena ndi mzake wamfupi uja as Gospel Truth timafuna mupewe izizi.K...
16/04/2025

Tikamanena k*ti don't take everything Tomaida Saka amanena ndi mzake wamfupi uja as Gospel Truth timafuna mupewe izizi.

Ku Zambia wina amamwa manhood enlargement k*ti k*ti toothpick yake izitolere.

Lero ndi uyu akulira k*ti chakula kwambiri.

ZOPEWEKA PEWANI.

Kukoma Kwa nsima sikuli mu kukula kwa mthiko koma mukatakasidwe kake.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mr Deeh. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category