Wadada

Wadada Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Wadada, Grocers, Mangochi, Blantyre.

new music from Mangochi
06/03/2026

new music from Mangochi

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

28/01/2026
21/10/2025

Blessed day

11/11/2024

DEKHA MTIMA WANGA [ Ndakatulo kuchoka kwa 13 Words ] 😝😝

Akumaimba foni
Nde tikumatha nkhani
Pena tikumachezera
Amvekere mwana uzandiberekera
Koma aaah!, dekha mtima wanga
Akaka sikoyamba kugwa mchikondi
Amaliza awa atapakula
Amaswa phale atakhuta

Mtima wanga dekha aka sikoyamba kuikidwa pa status yoona wekha
Zimachitika ndithu
Anthuwa ndi atambwali

Dekha mtima wanga
Ndalamazi ndi za banki mkhonde
Ndidziwa maluzi akuchapa
Kuthawira ku joni sichamuna
Kumene kuja chobwera mawa sichidziwika
Ena akugona diso liri gah!

Dekha mtima wanga ndi mwana uyu
Sikoyamba kuwona mwana wa mbina
Ndiwopalamulitsana anawa
Amachita kukuyamba dala
Cholinga upakule zikupote mmimba
Dekha mtima wanga

Mtima wanga dekha
Tiri pano ndi pa siwa
Mkazi ukufunayo ndinafedwa
Dekha mtima wanga iwe
Aka sikoyamba makoswe kundibera gondolosi
Pano ndi awa akungoti chwi chwi kudengaku aphanakotu

Dekha mtima wanga
Aka sikoyamba kulemba ndakatulo
Yofotokoza zomwe zatchuka

©13 WORDS

Address

Mangochi
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Wadada posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category