Tonde herbals MW

Tonde herbals MW We sale herbals and cosmetics products

TILI NDI MANKHWALA OSIYANASIYANA OTHANDIZA MAVUTO NGATI AWA:⁨0888 99 82 57⁩+265980785677🌿Ziphuphu🌿Spots🌿Stretch marks(m...
18/02/2024

TILI NDI MANKHWALA OSIYANASIYANA OTHANDIZA MAVUTO NGATI AWA:
⁨0888 99 82 57⁩
+265980785677
🌿Ziphuphu
🌿Spots
🌿Stretch marks(makandachembere)
🌿Kusalalitsa
🌿Kuyeletsa
🌿Kukulitsa tsitsi
🌿Kumeletsa dazi
🌿Kulimbitsa tsitsi
🌿Kukulitsa matako ndi ma hips(tea, capsules,cream,serum)
🌿Kukuza chida Cha abambo and many rounds(capsules, powder,cream ,oil,pills)

🌿Kuimisa mabele
🌿Kukulitsa mabele
🌿Kunenepetsa
🌿Slimming tea(kuphwesa thupi)
🌿Flat tummy. Tea(kuphwesa mimba)
🌿Kuthana ndi ma fibroids(zotupa za mimba)
🌿Mauka
🌿Likango
🌿Fungo loipa ku ndata, kubweza ndata, kuchosa madzi ku ndata

🌿Kubelekesa azimayi or azibambo omwe samabeleka
🌿Cancer
🌿TB
🌿Sugar
🌿Athrits
🌿Stroke
🌿Nyamakazi
🌿Mano
🌿Maso
🌿Mtima
🌿BP
🌿immune booster
🌿Ucers
🌿Gas
🌿Kuchokachoka kwa mimba
🌿Kupwanya kwa mafupa
🌿Fungo la nkamwa
🌿Zilonda za pa khosi
🌿kuchosa makwinya
Pezani ma herbal, mafuta, komanso zinali zambiri kwa ife

call/wap

+265888 99 82 57
+265980785677

Tikupezeka malo awa
Limbe,mzuzu, Lilongwe, mangochi (shop ili limbe fearmanillah building shop number 10, opposite police station or labour office limbe…….madera enawo kuli ma agent omwe muzikumana nawo ndikukatenga katundu….kutali ndimatumiza)

09800655540885079900Limbe C4 pillsMa tablets muli ma ingredients ama fruits and proteins.1.Amabweretsa mbina2.Amakungits...
20/01/2024

0980065554
0885079900
Limbe
C4 pills
Ma tablets muli ma ingredients ama fruits and proteins.

1.Amabweretsa mbina

2.Amakungitsa hip kukhala ya curve

3.Amafufumitsa miyendo (leg shape bwino)

4.Amachotsa ma stretch marks pena paliponse.

K15,000 only

Ma results amaoneka kwa 2 weeks ,100 percent guarantee.

Tipezeni ife kuti nanunso muthandizike

09800655540885079900Limbe Pali Azimayi ambiri mbiri amalakalaka kuti atatenga pakati koma ayi.Kuyetsera njira izi ndi iz...
19/01/2024

0980065554
0885079900
Limbe
Pali Azimayi ambiri mbiri amalakalaka kuti atatenga pakati koma ayi.Kuyetsera njira izi ndi izi koma ayi chete chete mwana osampeza

Ife takubweretserani ma tea bags awa

*Female fertility coffee tea*

👉 Amatsuka zoyipa za mchiberekero.

👉 Amabweretsa ukazi okhathamila bwino

👉Awa amapangitsa kuti ovarian carve ikhale ndi ya chonde kuti kukumana ndi umuna pompopompo kupanga fertilization yeni yeni.

👉Amachiza mauka omwe amakhala akuyabwa Ku ndata.

👉 Amachiza matenda opweteka Kwa period.

👉 Amapangitsa kuti ovulation ichitike bwino mopanda vuto lilonse ayi.

👉Amakhadzikika period normal bwino bwino.

👉Amachiza matenda opita padera anja.

*Kuti ukhale ndi pakati mosavuta pofunikila zinthu izi*

Tengani tea bag imodzi ikani mmadzi otetha mkapu kenako gugudila pakamodzi morning and evening.

Ma results amaoneka ukamatsatira ndondomeko imeneyi.

*Week imodzi mkazi amakhala kuti wasokonekera kale, zizindikilo za mimba zimayamba*

K18,000 only

Tipezeni Ife kuti nanunso muthandizike muchila, mukhale make Chembekezo

Traders of all natural wellness Ife tili ndi ma herbs awa*Azibambo*1.Kukuza chida cha abambo2.Kuwonjezera mphavu kuchipi...
15/01/2024

Traders of all natural wellness
Ife tili ndi ma herbs awa

*Azibambo*

1.Kukuza chida cha abambo
2.Kuwonjezera mphavu kuchipinda
3.Kumeletsa ndi kukulitsa ndevu Ku chibwano
4.Kuchotsa Tsitsi Pena paliponse.
5.kukhala ndi umuna okhathamila bwino opereka pakati.

*Azimayi*
1.Kukhala ndi ukazi okhwima okhala ndi pakati
2.Kuchiza zotupa za mchiberekero
3.kuchiza ma cyst, yeast infections,mauka, mabomu, chindoko.
4.Kukulitsa mbina
5.Kukulitsa mabere
6.Kuchepetsa mabere

*Zama cosmetics (mafuta)*
1.Oyeretsa khungu lonse
2.Kuchotsa ziphuphu, zipsyera, zikanga.
3.Kuchotsa njerewere, warts, keloids
4.Kuchotsa ma dark knuckles
5.Kuchotsa makandatchembere
6.Ochotsa zikang'a

*Ochiza matenda ama organs*
1.Ochiza matenda achiwindi, hepatitis
2.Ochiza matenda a Diabetes
3.Ochiza matenda alikango, Heamorrhoids
4.Ochiza matenda a Ipsyo
5.Kuwonjezera chitetezo cha mthupi

Komanso timachiza zizindikilo za matenda osiyana siyana

0980065554
0885079900
Limbe

*Kidney cleansing tablets towns wins*Ma tablets amphavu kwambiri pa nkhani yokolopa  Urinary tract system yonse.Whatsapp...
01/01/2024

*Kidney cleansing tablets towns wins*
Ma tablets amphavu kwambiri pa nkhani yokolopa Urinary tract system yonse.

Whatsapp
0980065554
0885079900
Limbe

1.Amachotsa miyala yama kidney (kidney stones).

2.Amachiza matenda opweteka kapamba komanso kupweteka Kwa mbali imodzi ya chiuno.

3.Kuchiza kupweteka ukamakozamo.

4.Kuchiza kuwotcha Kwa njira yodutsa mkozo, ngati muli tsabola.

5.Kuchiza matenda opweteka Kwa Malo obisika,ndata komanso kutsonga Kwa ndata.

6.Kuchiza mabala Aku Malo obisika prickly pear infections.

7.Kuchiza kutuluka sungu kosonga yotulutsa mkozo.

8.Kuchiza matenda ochepetsa njira ya mkozo.

9.Kuchiza matenda otulutsa mkozo onukha ngati fertilizer wa NPK,ukagoneramo.

10.Amasungunula komanso kuchiza matenda otulutsa mkozo wa magazi.

11.Kuchiza zizindikilo za mwela komanso kukonza mabatile kuti akhale mu normal shape.

K20,000 only

*Ma results amaoneka Kwa masiku ochepa basi 7 days results*

*Mamwedwe Ake samavutanso ayi*
✓Tengani ma tablets awiri morning, afternoon and evening respectively.
✓You will notice the best results.

Tipezeni Ife kuti nanunso muthandizike

*Kidney cleansing tablets towns wins*Ma tablets amphavu kwambiri pa nkhani yokolopa  Urinary tract system yonse.+2658889...
31/12/2023

*Kidney cleansing tablets towns wins*
Ma tablets amphavu kwambiri pa nkhani yokolopa Urinary tract system yonse.

+265888998257

1.Amachotsa miyala yama kidney (kidney stones).

2.Amachiza matenda opweteka kapamba komanso kupweteka Kwa mbali imodzi ya chiuno.

3.Kuchiza kupweteka ukamakozamo.

4.Kuchiza kuwotcha Kwa njira yodutsa mkozo, ngati muli tsabola.

5.Kuchiza matenda opweteka Kwa Malo obisika,ndata komanso kutsonga Kwa ndata.

6.Kuchiza mabala Aku Malo obisika prickly pear infections.

7.Kuchiza kutuluka sungu kosonga yotulutsa mkozo.

8.Kuchiza matenda ochepetsa njira ya mkozo.

9.Kuchiza matenda otulutsa mkozo onukha ngati fertilizer wa NPK,ukagoneramo.

10.Amasungunula komanso kuchiza matenda otulutsa mkozo wa magazi.

11.Kuchiza zizindikilo za mwela komanso kukonza mabatile kuti akhale mu normal shape.

K20,000 only

*Ma results amaoneka Kwa masiku ochepa basi 7 days results*

*Mamwedwe Ake samavutanso ayi*
✓Tengani ma tablets awiri morning, afternoon and evening respectively.
✓You will notice the best results.

Tipezeni Ife kuti nanunso muthandizike

Address

Blantyre

Telephone

+265885079900

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tonde herbals MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category