Zathu zomwe

Zathu zomwe No any one

21/11/2022

Inetu sipitara uja amakulelani mokuyeyekani! ine mukhawula ndikukwela kwazinthu . munya muona mpaka 2063 .

pitara uja amakusasatitsani km ine ndichilima tikuphuzitsani kulimbikila!

14/11/2022

Tsopano nthawi yakwana Ndipange za one million job zija ,

Ndikuona kuti achimata akuvutika tsopano!😓😓😓

13/11/2022

Ndikuzivera chisoni amalawi! Coz palikagulu kena kochokera ku Mcp kms adpp! Ndisakubisileni Amalawi! anthu amenewa akufalitsa nkhan zabodza .

Eti akumanena kuti ndidatchola nthiti ziwili zankaziwanga . Kmt ineyo zikundinyasa coz iwowo azachipatala aku India akunena xankutu Kungofuna kundiyipitsila mbili cholinga 2025 ndisawine .

kms ine ndafana oganiza boh Ndipo sizingatheke Kthyola nthiti ziwili zamwana kuwala wanga Mary chilima!.

Pomaliza ndingot Ine ndiwama computer ndikusakani . Km ndazivera chisoni 😭😭😭

09/11/2022

Mzimu waumulungu udalipodi mwa jeni ansar! km satana sadalole mpakana kupanga chilichonse choti Peter muthalika achokedi.

Lelo tikulila mayi athu Inu . Amalawi mudatikonda km kusava plus umphawi umbuli watumbuka ndi achewa omwe Ndiomwe waika dzikoli pamoto .

zokamba zambili tilibe mayi; km kwathu ndikulila Basi 😓😢😥😩🥵😭😭😭 Amalawi misozi yosatha.

Address

P/o Box 52
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zathu zomwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category