03/12/2021
Amene muli kumademo kumpoto plz tapotananu pitani ochuluka ndithu born amuuza kuti udindo samupatsa komano boma langotsitsa zinthu zomwe zakwelazi komano udindo born sapatsidwa nde tikudziwa tonse kuti chiyambi chankhaniyi chinali choti akufuna udindo m,boma nde tiyeni tionetse kusakondwa inde zinthu zitsika komano born unduna amupatseπππππ