Chilungamo general dealers

Chilungamo general dealers Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chilungamo general dealers, Grocers, Lilongwe.

23/02/2026

JUSTICE AGRO-DEALERS
kupanga malonda okomera aliyense ⚖️

TIKUGULA CHIMANGA PA MTENGO WA 1150 KUZUNGULIRA LILONGWE MSIKA WA MBEWU Msika wa fodya Msika wa mbeu MUZIBWELETSA PA MA ...
14/01/2026

TIKUGULA CHIMANGA PA MTENGO WA 1150 KUZUNGULIRA LILONGWE MSIKA WA MBEWU Msika wa fodya Msika wa mbeu MUZIBWELETSA PA MA TRANSPORT ANU.

19/09/2025

DPP WOYEEEEEEEEE

SOYABEAN MK 2000/KG
10/05/2025

SOYABEAN MK 2000/KG

10/05/2025

JUSTICE AGRO-DEALERS
( Kupanga malonda okomera aliyense ⚖️)

10/05/2025
25/04/2025

MR MUMBA MUTIPWETEKETSA ZOONA

ZIGANIZO ZIKUMAPANGIDWA MUZIGANIZIRASO MBALI ZONSE.

1. ZOMWE ZINGAKHUDZIDWE.
2. ZOTSATIRA ZAKE - ZABWINO KAPENA NDI ZOIPA.

KUNENA ZOONA AMA BUSINESS YA AGRO-DEALERS MWATIPWETEKA KWAMBRI KOMASO ALIMI APHEDWA APA.

TANZANIA NDI DZIKO LIMODZI LOMWE TIMAPANGA NALO BUSINESS ‼️

OGURA KOMASO NJIRA ZATHU ZILI KUMENEKO.

NEXTIME PLEASE ZAUNIKILENI KAYE

TAONA POST YA Triephornia Thomson Mpinganjira ZOKHUDZASO KWAMBIRI.

Azathu ama business a mbeu tiyeni tipange ziganizo mwa changu zotsegula njira yanthu.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chilungamo general dealers posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category