Zili kuti zotchipazo

Zili kuti zotchipazo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zili kuti zotchipazo, Grocers, Lilongwe.

With Ida Chicker Chabs – I just got recognised as one of their top fans! 🎉
29/04/2026

With Ida Chicker Chabs – I just got recognised as one of their top fans! 🎉

With Joyce Kumvana Kaponda – I just got recognised as one of their top fans! 🎉
29/04/2026

With Joyce Kumvana Kaponda – I just got recognised as one of their top fans! 🎉

27/04/2026

ANTHU AKULIRATU KU MALAWI

Hello sir I was watching your video about mayi zione Diana from mzuzu the ladies my name is ABGAIL (not real name) a student at poly I can say me and my family we are going through the same thing.

kwathu tinaliko 6 now we are a family of three me my mom and my big brother both of the two sisters died and my father too. so after my father passed away we got his pension money he was a police officer my mom invested that money and started a family Bakery business.

it was small but we were living at that time the bakery was at mangochi boma because zithu sizinayende we had to move to Lilongwe kuti mwina that was 2024 after a while things started getting better matumba aliwi a flour amatha pa day zithu wezi wezi getting better then in 2025 a MBS came Ku bakery they closed it for same days then reopen again but we paid around 500k after some months a city anabwera you know how they go about ati ma paper tilibe bwa we gave them 270k for the papers and everything guess what

MRA anatulukila anatiwuza zambili kuti atseka Chan Chan koma they need 500k we did just that a bakery that will makes 1 or 2 bags of flour but athu awawa they are demanding alot from us and I don't know if all these big bakeries amatelo .

Just yesterday I received a call from my mom kuti kwabwera a Lilongwe city akufuna 1million from the same business yoti we can't even make 500k pa tsiku as of now we are thinking of just closing it coz we can't afford all this Bills and my school fees ikuchokela pa the same business koma these people want more than the business as the only daughter I don't know who to ask for me or who to call because this is the only source of funding to my family thank you nangoganiza to share with you this story coz many of us we are suffering because cha athu ngati awa

HOW CAN WE FIX MALAWI?

27/04/2026

Miracle Vic Chinga

26/04/2026

Ma nyumba ambiri panopa mitengo akupanga ndi ma agent osati landlord cholinga chawo ndikupeza commission ya mbiri.. Samalani nawoni anthu amene. Ma landlord ngat muli ndi nyumba za rent inbox

22/04/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Eunice Sulamoyo Kambalame, Anderson Andrew Mangani Chimasula, Binali Chitenje, Yankho Carthy Banda, Fabiano Chawinga, Joyce Kumvana Kaponda, Ruth Chisomo Thole, Real Martha Wa Gomonda, Lusungu Zimba Maononga, Thoko Kachale Kash*tigu, Lindiwe Stock Dandize, Maria Kapichi, Henrie Kamie, Matthews Kanyenga, Mdex Timothy, Limbani Magola, Alice Chikhambi Wa Geya, Alima Kanyenda, Rose Perpetual Malinda, Iless Singini, Naamah Mtende, Mercy Zulani, Ruth Nkhoma, Desire Thomas, Anna Chasowa, Tapiwa Jamu, Alex Kabango, Samuel Katandika, Madalo Crey Nkata, Judith Kapesa, Flossy Chapola, Maga Ni Zo, Akim Banda, Brighton Cool Kusseni, Dauka Manondo, Sandrina Chitende, Zauna Kalinga, Na Chilenje, Jane Chinangwa, Grace Banda Banda, Hanifah Ahmed, Linda Maps, Henrietta Kamata Jentala, Patrick Damson, Imed Batson, Enifa Lion, Brenda Kameta, Veronica Bush, Matilda Kondowe, Doreen Mwafulirwa

22/04/2026

Ma landlord ngat mukudziwa kuti muli ndi nyumba za rent tipezeni ku inbox kuti anthu akupezen ma agent akuba kwambiri mu dzina la zithuz

18/04/2026

With Miracle Vic Chinga – I just got recognized as one of their top fans!

17/04/2026

*Mkazi wa chibwezi kuti upange naye chipako:*
1. Transport ya go and back umtumizire.
2. Ndalama umtumizirenso yoti awasiyile ana ake.
3. Ulipire ndalama ya room komanso kukuwerengera ma hours.
4. Akupase matenda.
5. Ugule zakudya zoti mudye mu room.
6. Mukamalizanso kupanga chipako umpasenso ndalama zina.

*Mkazi wabanja kuti upange naye chipako:*
1. No transport.
2. Ngati wampasa ndalama mudya nonse limodzi.
3. Palibe kulipira room.
4. Palibe kukupasa matenda chifukwa mumakhala kuti mukudziwana kale.
5. Palibe kumulipira. Upanga chipako mmene ungafunire.

*Tiyeni tisankhe chimodzi azibambo chifukwa pali mwambi wakuti:*
"Mapanga awiri avumbwisa."
"Pawiri pawiri sipauzilika."
"Ichi chakoma ichi chakoma pusi anagwa chagada.

16/04/2026

I'm on the weekly engagement list for Mikozi and Miracle Vic Chinga.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zili kuti zotchipazo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category