Killer of story kell ce

Killer of story kell ce Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Killer of story kell ce, Grocers, Lilongwe.

25/04/2023

OFF LINE GUYS

13/04/2023

Kaya moyo ulibwanji ma bwana ndi ma dona aaaa ine moyo wa nthazi koma mongokumbutsana kuti tili munyengo wa achikondi ๐Ÿ’•๐Ÿ’• cha and this is part 2 form to

Killer of story kell cee
Koma tisanayambe kuwelenga chonde onetsesani kuti mwapanga SHARE komaso Like then follow my page

Gift asanayakhe anazizumuka kumuona tsikana wowala bwinoyi ndimene akaonekela mogonetsa ndipo mpakana anangouma mwana wa nyamata ndipo

tsikana anafusa kuti tikuthandizeni

Gibo eya ndimafuna madzi Akumwaaa koma ndingafuseko pang'ono kaye

Tsikana eya m***a kufusa mati bwanji?

Gibo pepan ngati ndingalakwise adona kodi dzina lanu ndinu ndani?

Tsikana sananyade anamuusa kuti dzina lake ndi Sarah koma mondinyadila Amangoti ndi Sali

Gibo eeee muli ndidzina lokongola ndiposo ngati palibe amane anakuuzaniko eeeeee adona ndinu okongola

Ndipo tsikanayo pokumva dzimenezo anasangalala mu mtima mwake ndipo amadabwaso kuti mawu amenewo akuchika nkamwa mwa nyamatayi ndipo naye anamufutsa nyamatayo kuti

Sali nde iwe dzinalako ndindani

Pamene nyamata akafuna kuti amuuze dzinalake tsikayayo kunapezaka kuti amayi ake anamuyitana mwachangu tsikanayo ndipo sanatheso kumwa dzina la nyamatayo

Gibo ndineee Gii

Tsikana uja basi akundiyitana nde ndikangokutengela madziwo nde kuti dzina lakolo uzanenabe tsiku lina wamva

Bibo chabwino

Ndipo anakamutengela madziwo kupasa a Gibo anabwelera kumaka kumba Zenje la chimbuzi lija koma mene akakumba akangoganizabe ndimene amaonekela๐Ÿคฉ sugwana uja eeeeee kujaku asikana nde alipodi koma sinaoneko tsikana onga uyu ndipo Gibo anakhala kaye pheee kudya mutu๐Ÿค”๐Ÿค” ndipo ine tsikana anene uja takhala kuti ndikufuna angandilore k**a been ngati ine? osowa pokhala omangokhalira ma ganyu? Ndiposo ndingapase chani nkazi ngati ameneyi eeeeee? Iyeyu si stutes yanga ndipo akufunika Amuna Achuma Azindalama ๐Ÿ’ถ๐Ÿ’ต๐Ÿ’ด๐Ÿ’ฐ๐Ÿ’ฐ zawo koma osati ine singamake bola ndingozitaya et

Amenewo anali maganizo anyamata uja

Next.........

Please share this mypag.

12/04/2023

Yes guyz takumanaso munyengo inono ya achikondi cha GIFT and SARAH kodi zinakhala bwanji kuti anthuwa Apangane mapangano kapena kuti ngwilizano nde chonde ngati mukuyipanga follow nkhani pangani Share komaso like kuti nkhaniyi izikupezani mosamvuta This is

Part1 from to killer of story

Kalekale mudzi wamulanje mudali nyamata wina yemwe anthu ambiri amamudalira padzomwe akachiti kumuziku ndipo nyamatayi anali ndi mankhalidwe abwini komaso anali othamanga nthamanga ku magwira zintchito zammNja iyeyi pakomo lakwawo sikunali kochitabwino or pang'ono pomwe koma saname nyamatayi amayesetsa kuti Azikhala moyo wosangalala ngati nyamata iyeyu amagwila ma gobo makomo Awanthu osiyana siyana mudzimuu ndipo moti athu ambiri anka..dalira muzambiri ndipo tsikulina Gift anamuyitana kunyumba ina kwankulu wina yemwe anali nkhumuntcha kapena kuti ochitabwino pa chumu yemwe amadziwika kuti MR Namahala ndipo MR namahala anali taswungwana tiwiri Jenne and Sara Anali asikana opasa chidwi awo asikana wokongola ngati Adziko lomwelino ra Malawi eeeeee ndipo Gift anamuyitana kuti akakumbe chimbuzi kunyumba yankuluyo ndipo anapitadi kukagwila ntchitoyo Giftyo

Ndipo Tsiku limenelo Gift Alinkati mokumba chizenje lachimbuzi poti kunjaku tsiku limenelo kudali dzuwa๐ŸŒž kwambiri ndipo chifukwa chakutopa anayamba kufuna madzi ludzu linamu wawa ndipo ananyamuka kupita kuseli kwanyumba bwana Namahala ndipo anepeza kuti anthu alinyumba anafuna kuti Agogode pachiseko ndipo anagogodadi ndipo amene anatuluka Anali SARA sara tamva kugogoda tikuthandizeni ngati?

Gift asanayakhe anazizimuka kumuona tsikana wowala bwinoyi akuoneka mogometsa ndipo mpakana anangouma Mwana nyamata ndipo tsikana anafutsa kangapo kuti tikuthandizeni

Next........ tangoyiyambapo pamenepo fire๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ kodi chifukwa chani Gift Atamuona tsikanayi anangouma eeee osayiwala Share komaso like pageyi chonde

09/04/2023

Tomorrow tikubwela ndi
mapangano Eni Eni Achikondi
A GIFT And SARA
Kodi mwakozeka???

08/04/2023

๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ
Mapangano Gift and Sarah
coming Soon ๐Ÿ˜ฑ๐Ÿ˜ฑ
from to killer of story kell cee
Are you ready๐ŸŽบ๐ŸŽบ

07/04/2023

Mwabwela

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Killer of story kell ce posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category