12/02/2022
🙆♂️The Twin brothers 🙆♂️
Written by alick
Sponsored by Joseph
Chapter 3
Tinasiira pak*ti Erick amafuna andiyankhule 👉Avekele
Continue 👉👉bro msafooke ndipo pitilizan potengera ndimene wanenera iyeyo ndizoveka Kma osagwera ulesi.. Brother mwamva??
👉Ndinangovomera basi pamenepo ulendo uli Kati kupita Ku nyumba mosakhalitsa tinafika, kenako ndaipanga pack galimoto ija,, kenako tinalowa nyumba ya uncle Innocent mix ndiamene anapanga ka party kenakake mdziwanso moyo umakoma ndi zinjoy kukamba za uncle Inno anatipatsa malo Tina khala posakhalitsa,,, uncle Inno anabwretsa mowa k*t Tisangalale,, kukamba mosabisa Zinthu zinali bho heavy kaparty katatha Ine. Ndinapita pomwe,, panali nchimwene uja. Ndikumgwra pankono 🤝k*ti tizivaya,, posakhalitsa Tinatsanzika kwa uncle Inno k*ti,, tikuvaya Ine ndi Erick tinanyamka k*ti tizipita after party Erick analezera modetsa nkhawa kwambiri,, chokha chongotuluka ndik*ti ndizitsekura chitseko cha galimoto,, ndinangodabwa uyu aness "watulukira kumpanda kuja kma - ali pa liwiro loopsya 🏃♀️ine ndinangodekha pheee pa galimoto ija,, kenako anangofikira kundikwenya malaya womwe; ndinavaya kma Mau oti chonde alick ndithandize,, ndili mumavuto ine,
Posakhalitsa kunatukira anyamata 7 ali ndi zida mmanja kma ine ndinangodekha 🙇♂️
Ndinamva Erick mchimowa mowa ali kd bro kwabwera mumu kd??? Ine sinamyankhe posakhalitsa madolo aja,, anafika pomwe ndinali ine
Avekele heeey mfana tasuntha ife tikufuna nkazi bwana wathu.. Ndiamene watiuuza,, ine ndinangomtenga aness uja ndikukoka m galimoto pamene, ndimamaliza kuseka chitseko ndinalandira fight🤜yomwe inandigwetsa k*tali, Ine posafuna kundivulaza ndinauuka nd headspling yomwe ndinakafika ndi back kma yoopsa🤸♂️ndinamenya mmodzi mwa iwo kma ananyamuka ndi kugwera Mutu osadzukaso a zake ;,, onse Anandithawa.. Ine ndinangilowa mu galimoto ija ulendo wayambika,,, tili mkat mwa ulendo ndinayamba,, Kumufunsa chifukwa chomwe " amafuna kummenyeracho kma mmalo,,,,, like and comment share