14/05/2026
Ndadza ndi mafunso
1. Pakanthawi, nkhani yakuti US ikufuna kutenga Greenland ilinkamwa nkamwa, ine ndinanena kuti sizingatheke munthu kulanda ma Europeans dziko ku Europe konko.
Iwowa ndi amene anakonza game Yolanda ndi kupanga colonise mayiko.
Ambili anandiwowoza, ena nkuti ndikaphike ndi mzimayi.
2. Itayamba Iran, US ndi Israel kupanga attack. Ime ndinakhala ndikunena kuti, anthu a ku Persia (Iran), ndi ovuta, amadziwa strategy, iwowa nkhondo yawo ikhala economic war, ndipo ali ndi system yovuta kugwetsa.
Ndinati, empire yawo yapanga exist kwa 6000 years. Ndipo enawo, avulala somehow.
Ambili anandiwowoza, akuti umadana ndi amerika, sukudziwa kanthu, ena nkuti kaphikr ndiwe mzimayi.
Nde ndinali kophika ndinasiya kukamba, ndabwerako....
Ine ndimangokamba zili pa ground, kulumikiza ndi History where necessary.
Please telo mi.......zili pati?