Nkhani za m'mudzi wa kamdidi village.

Nkhani za m'mudzi  wa kamdidi village. Good luck

23/11/2023

Akuti onse amene akuti a kamdidi akale omwe timaziwa tonse achokepo anyamata omwe sakulora kuti ukamdidi upite kwa wina ayankhula kuti onse omwe akufuna kulanda ufumu wa kamdidi village nawoso akhale ndi ma shopu awo ndikomwe azigura katundu koma zili kuno mmmmm ndikhani dzina.

23/11/2023

Amene Ali mwana wa a kamdidi chirwa pankhaniyi amutchula yemwe anamutaya muchidebe chamadzi last week. Mwati ndi ndani pajah..... 🤣🤣🤣🔥🔥✍️

23/11/2023

Ndiye mwati wina anamutaya muchidebe chamadzi chifukwa chakuti anawarozela alendo kumalo alakwika kumene wina akuzitcha kuti aranda u kamdidi. Ma Guys angakhale ndani yemwe anamutaya muchidebe chamadzi last week. Koma Mr luso chirwa mmm ulem wanu.

23/11/2023

Kodi nkhan iyi mesa ndiyoona et.

23/11/2023

Za vuta kuno ufumu uja amati avala lachisanu likubwerari akuti wakanika et.

Tiyankhulene mwachangu madzi asanafike pakamwa because apa Ali mukhosi.
22/11/2023

Tiyankhulene mwachangu madzi asanafike pakamwa because apa Ali mukhosi.

Tiuzene mwachangu lisanafike lachisanu likubwerari Kodi amene akufuna kulanda ufumu wanthu wa A kamdidi titani nawo. Tisatira mau Anu.

Tiuzene mwachangu lisanafike lachisanu likubwerari Kodi amene akufuna kulanda ufumu wanthu wa A kamdidi titani nawo. Tis...
22/11/2023

Tiuzene mwachangu lisanafike lachisanu likubwerari Kodi amene akufuna kulanda ufumu wanthu wa A kamdidi titani nawo. Tisatira mau Anu.

Koma mudzi was kamdidi village ndi nkhani dzina mmmmm
22/11/2023

Koma mudzi was kamdidi village ndi nkhani dzina mmmmm

Pamene tikuti takhala ndi too days only kuti china chake muno mmudzi wa kamdidi village chichitike.
22/11/2023

Pamene tikuti takhala ndi too days only kuti china chake muno mmudzi wa kamdidi village chichitike.

Address

Kasungu
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani za m'mudzi wa kamdidi village. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category