Cee Lom

Cee Lom Songwriter, singer, dramatist & actor

04/05/2025

Hie guys , zik*ti bwanji kumeko

Just to announce that something new it's been cooked n to be released soon
Will be available in some popular Malawi platforms
It's me Cee Lom like n follow my page 4 more Cee Lom

13/02/2025

Being silent for a while now I just wanna say dat something good is being cooked πŸ€«πŸ‘€πŸ’«πŸ”₯

20/12/2024

Hawau wikisians πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ€£πŸ˜‚πŸ€£

Proud to hear this new idea WikisWikise1992enafe tikhala ndimaina ambiri
Achina Teddian, Driemonian,

20/12/2024

Breaking News😭
Sad news 😭😭
Zachitika pompano mtsikana yemwe amatsogolera nyimbo za great angels uja ,nyumba yake yachita ngozi ndipo yayaka moto ,ndi izi zachitika iye ali mnyumbamo momo kulephera k*tuluka ,anthu ena akuyesesa k*ti amupulumutse ,koma moto ndi omwe waonjeza kwambiri 😭😭 mlongo wake yemwe amayimba naye limodzi nyimbo uja wakwiya kwambiri ndipo akufuna akalowenso naye mnyumbamo angopsyera limodzi ndi mtsikanayo koma mwamwayi apolice atulukira mwachangu akumuletsa mlongo wakeyo k*ti asakalowe mnyumbamo ndipo pano pavutiratu sindikudziwa k*ti zitha bwanji....izitu zikuchitika mu nyimbo yawo ya great angels choir video ,mutu wake wa nyimboyi amati MUSALORE ,Tikuyionera pa screen nyimboyo yili mkati siyinathe ,khalani pompo tikuudzani zambiri mmene zingathere ,nyimboyo yikatha zikomo😏😏
Tadinani apa πŸ‘‰ Cee Lom Cee Lommupange follow n like k*t ikatha ndikuuzeni ZambiriπŸ€£πŸ˜‚πŸ€£πŸ˜‚

02/12/2024

To those we discussed about projects please send me message on wap or call on +265883220291, I'm sorry I lost my contacts

Thank you all for your attention

Address

Lilongwe Capital City
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Cee Lom posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category