MADKA page

MADKA page Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from MADKA page, Grocers, 0991722008, Lilongwe.

05/12/2024

KUNAVUTA KU PARLIAMENT PAKATI PA NAMALOMBA NDI CHIMWENDO.

NAMALOMBA: ndikanakomda a zikhale ng'oma akanapezeka Muno lero.

CHIMWENDO: atani azikhale ng'oma wo?

NAMALOMBA: ndiwafuso mafuso Ngati nduna yazachitetezo.

CHIMWENDO: ndifuseni ineyo ndiwayankhira Monga mmodzi mwa nduna zaboma.

NAMALOMBA: ok ndikunva Kuti mukumanga nyumba Za apolice nziko Muno?

CHIMWENDO: eya bwanji?

NAMALOMBA: ok ndimafuna ndikuuzeni Komanso Ndiku kumbutsani Kuti pamene mukumanga nyumba Za apolice "Mukonzeso ndende zaziko lino cholinga next year mukachoka m'boma mukafikire ndende zabwino " zikomo 🏃🏃

CHIMWENDO: what??????????????????

05/12/2024

Zina zomwe wayakhula Temwa Chawinga
1 COSAFA ndimpikisano wama local players
2 ak*ti Fam iziyika chidwi pampikisano ikulu ikulu monga AFCON , WORLD CUP

Mmene amayakhula izi amadandaula k*t thandizo azipeleka mofanana ku Flames komaso kwa iwo
Compiled by Brian kamatora Shaba

05/12/2024

There is God in heaven let's prepare this day of his coming

04/12/2024

Kod anduna azatchumawa ak*t chan

07/08/2024

Mwaswera bwanji athu nonse muno

Address

0991722008
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MADKA page posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category