27/05/2024
Nyimbo yabwinodi imaziphusha yokha
Ndikudabwa kuti Mikozi ndi Makosana sakuwapopa bwanj adha awa pa achievement yawoyi.
Komano penanso ndikudabwa kuti ma fans ake ndi akutiko amene amaonela kuti ifike ma views choncho chifukwa nyimbo yokuti ili 981k kusala ndi 19k kuti ifike mita anthu sakuiziwa bwanj.
Kayo withu watizizimusa
https://youtu.be/QrdOl3dc2J4?si=DREMaez_1Ff_jESO