Nyumwa

Nyumwa To entertain and educate each other

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Stevo Kasonde, ยิ้มแย้ม แย้ม แจ่มใส, Dan Toy
17/12/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Stevo Kasonde, ยิ้มแย้ม แย้ม แจ่มใส, Dan Toy

13/12/2025

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

15/11/2025

Gwadza part 1

Apongozi athu ayimbiiidwa nyimbo...odala ndi Iwo ndithu 🙌🙌... Fresh Døn Abebu  iweyooo😂😂Ife tioneke ngati athu tilibe na...
13/05/2025

Apongozi athu ayimbiiidwa nyimbo...odala ndi Iwo ndithu 🙌🙌... Fresh Døn Abebu iweyooo😂😂Ife tioneke ngati athu tilibe nawo Ntchito eti??...wawina.. link iyi ma guy👇

https://youtu.be/rJhs-25I11o?si=FNTYnf_JlF6VUIMV

Uyu ndi munthu amene wachka masamba antchedzo mu ziwaniko dzochepa dzankuluyu ndindani amatani nanga walakwanji tiyeni o...
12/05/2025

Uyu ndi munthu amene wachka masamba antchedzo mu ziwaniko dzochepa dzankuluyu ndindani amatani nanga walakwanji tiyeni osaiwakupanga nyumwa
1- uyu ndi Elijah sinsika Dukama, ndidzika ndithu yamaiko awiri omwe Ali malawi 🇲🇼 komanso South africa 🇿🇦
2- Nkuluyu makolo ake anskomana ku South africa komwe bambo ake anapita kogwira ntchito ku South africa ko . Mai ake ankuluyu ndi thrubeg tseppo ndipo kwao ndi Dela lina lochedwa Johnsburg town otchedwa kuruman.
- Bambo ake ankuluyu ndiochokela ndziko la malawi bola la nzuzu
- Bamboyu atapita ku South africa kogwira ntchito yamigod anakomanako ndi Mai ake ankuluyu ngati ogwira naye ntchito
- ndipo muubwedzi wawo anapasanapo mimba ndipo mwana atabadwa Mai ake a amutenge nawapasa bambo ake kuti banja latha moti nthawi imeneyo nkuluyu Ali ndzidzaka 9
3 -Nanga nkuluyu watani nkuluyu akuganizilidwa kuti wasokonedza Malo Ena omwe amagwirapo ntchito ndi ndzake wa business ndipo iye wathawa ndi gawo lina la business yankulu wina wopanga malonda mu lilongwe mu area 25
- Ndipo nkulu wa ma business wanenesa kuti kwayemwe angadziwe kapena kmuona kwina kwake alandila photo yachiona maso chokwana 23 million kwacha
- Ndalamayi imafika apa chifkwa munthuyu sakupedzeka ndipo ngati angapitirire kusaoneka ndikukhulupirira kuti ikwela
- Funso nkumati omuona kapena kunena kuti angamugwire alandila 23 million iyeyo wathawa ndidzingati
- kusauka ndikufuna uwu ndimwai waine ndi inu kuti tiiphule apa
- Iyi ndi information yochepa yankuluyu

Breaking New's Zigawenga zomwe zidatchinga pa Mponela m'boma la Dowa ndkuotcha imodzi mwa Galimoto ya DPP pa mdipiti wa ...
12/05/2025

Breaking New's

Zigawenga zomwe zidatchinga pa Mponela m'boma la Dowa ndkuotcha imodzi mwa Galimoto ya DPP pa mdipiti wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa DPP m’chigawo chapakati olemekezeka a Alfred Gangata pamene amachokera ku nsokhano ku ntchisi zagwidwa kucha kwa lero.
Isaac Kalima ndimodzi mwa chigawenga chomwe anthu adachizindikra nkhope a Norman Chisale atapeleka report za Munthu oganizilidwayu adapita usiku kunyumba kwake komwe adayamba kuyakha zosaveka a Police atagwira ntchito yawo mwadongodolo Bambo Kalima adawulura ena mwa anzawo omwe adali limodzi.
Mneneli wa a Police a Peter Kalaya asimikiza za nkhaniyi kunena kuti Agwira zigawenga zisanu zomwe zidali ndmifuti itatu zikwanje ndi nkhwanga.

A Police asimikiza kuti imodzi mwa mfutizi ndiyomwe adagwilisa ntchito powombera min bus ya chipani cha DPP. Anthuwa avomeleza mlandu wawo koma ati awakhululukre chifukwa adachita kutumidwa ndi anthu ena andale.

Low place
22/03/2025

Low place

Address

M Baluku
Mangochi

Telephone

+265885834932

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyumwa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category