Udon Dairy

Udon Dairy Healthy dairy products produced by UDON Dairy in the greenest City of Malawi, Mzuzu, in Kaning'ina, distributed across Malawi and the neighbouring countries.

Good Morning Mbali ya kumeneko akaka mwakalawa liti? Pangani share Kwa anzanu kuti yogurt ndi WITHU ndipo ma share akach...
07/05/2026

Good Morning

Mbali ya kumeneko akaka mwakalawa liti? Pangani share Kwa anzanu kuti yogurt ndi WITHU ndipo ma share akachuluka tigawanapo bundles pa mudzi pano

yogurt Dairy

Mwadzuka bwanji pa Sunday Anzanu nyengo ya holiday ino akumwa WITHU yogurt ndipo ambiri akuchitira umboni za kuzuna Kwa ...
05/04/2026

Mwadzuka bwanji pa Sunday

Anzanu nyengo ya holiday ino akumwa WITHU yogurt ndipo ambiri akuchitira umboni za kuzuna Kwa WITHU

Pezani wanu lero kuti nanu musangalale nawo nyengo ya holiday ino

yogurt
Dairy

Chilobwe United Football Club in the gym. Kapena mufuna yoghurt?Zimafunika healthy food izi.    Dairy
25/03/2026

Chilobwe United Football Club in the gym. Kapena mufuna yoghurt?

Zimafunika healthy food izi.

Dairy

Happy Eid Mubarak everyone.
21/03/2026

Happy Eid Mubarak everyone.

Good Morning WITHU yogurt alipo mu nyengo ya FA Cup quaterfinal yiKodi watola joker ndi ndani?   yogurt  Dairy
10/03/2026

Good Morning

WITHU yogurt alipo mu nyengo ya FA Cup quaterfinal yi

Kodi watola joker ndi ndani?
yogurt Dairy

06/03/2026
Mwaswera bwanji?Kunja ndi Kwa dzuwa uku, koma lero WITHU YOGURT mwamulawa?   yogurt  Dairy  brand
05/03/2026

Mwaswera bwanji?

Kunja ndi Kwa dzuwa uku, koma lero WITHU YOGURT mwamulawa?

yogurt Dairy brand

Everyone wants a taste of Withu Yoghurt
05/03/2026

Everyone wants a taste of Withu Yoghurt

Amati chiyani plug yo akumakukakamizani fake outfit?Get the latest and original outfit at AJ's Fashion
22/03/2025

Amati chiyani plug yo akumakukakamizani fake outfit?
Get the latest and original outfit at AJ's Fashion

Address

Kaning'ina
Mzuzu
00265

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Udon Dairy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share