23/07/2022
Malingana ndikuvuta kwa zinthu tayamba kugulisa chimanga,mapira, madeya opasila ziweto komanso madeya oti anthu akhoza kudya, mitama yachimanga yochokera kumakampan,makaka osaiwalanso ufa wa makaka anthu ophika mowa wamasese,chikokeyan bwerani chifukwa ufawu ulipo wambiri wabwera wanyuwan simuzakhumudwa tipezen ku ofesi yathu kwa jojii trading centre ku MPASA munyumba ya aTA jenara manambala afoni ndi awa 0998143529/0884456785/0887243529 muzalankhula ndi eni ake aMpinganjira mpaso bwana wa chinyamata womva madandaulo a anthu KOMANSO TIMAPEREKA UFA WOPANGILA MABISIKET KUMAKAMPAN.