Zochitika Mwa Chisinkha

Zochitika Mwa Chisinkha Sitikamba maboza koma zochitika Mapanga sec school inatipindulira

Nolani Mano, komanso konzekerani kuzadikura chifukwa mmudzi muno madanko nde sakutha.Moto kuti buuuuThira kukwatira Alib...
11/07/2024

Nolani Mano, komanso konzekerani kuzadikura chifukwa mmudzi muno madanko nde sakutha.

Moto kuti buuuu

Thira kukwatira Alibe
Chabwera kukwatira Meve
Muhuwa kukwatira Charity

Inu Ali ndimwana agwilise.

30/06/2024

Mmudzi mukubweraso mwana wina yemwe akufuna kuyimira ukhansara uyu ndi Dominc Chikopa.
Sopano list ikukura ndithu
Fanuel khuzupa
Chipilro Dowesi
Domic Chikopa
Khasara malata samala anawa sakubwera mocheza.

11/06/2024

Chipwilikiti mudzi pomwe akazi akhoviwa amukomora Linire chifukwa cha msanje abare kumudzi kunotu kwavuta.

02/06/2024

Ize wa nickson wamenyana ndi witi yemwe amatchuka kuti wigoh khani zake ndizifukwa zakarekare pajatu anthuwa amanyenga mkazi mmodzi.

20/05/2024

Kaufera khoviwa.,mkamwini wa akhansara komanso malizani wa kwa mg'omba ndi anyamata omwe apita kujoni opanda mapasipoti mokuti pano agwidwa Ali pa belt Bridge kufuna kuomboledwa.

Zochitika mwachisikha muno.

Tidziwe izi๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡Kudera kuti kufike chitukuko Zimatengera MP wa kudelaro kuti asayinire ntchito yonseyo kenako MP yemweyo nd...
16/05/2024

Tidziwe izi๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

Kudera kuti kufike chitukuko Zimatengera MP wa kudelaro kuti asayinire ntchito yonseyo kenako MP yemweyo ndiyemwe amapeza contractor oyendesa chitukukocho.

Khansara samapita ku parliament kotero iye amapita ku Assembly zimene zikusonyeza kuti khansara atakhara kuti wapempha chitukuko ku Assembly nde amupasa pafunika MP asainire ngati sizitero chitukuko sichifika.

Bridge yomwe yamangidwa mmudzi mwathu tikungoona kudana ndi khansara malata koma sichoncho ayi bridge ija wamangisa ndi mchacha monga MP. Malata kwake kunangokhara kungooneera monga chitukuko chokuti chili mmudzi mwake.

Malata Bridge ija sikumukhuza chifukwa olo contractor anamangisa uja anapeza ndi mchacha mosogozedwa ndi adindo ena ammudzi.

Malata sanalephere pampando wake koma kuti anthu akusogolowa sanam***andize chifukwa sanathe kusainira zitukuko zina. Bridge imeneija ikanakhara kuti ndiyolongosoka ndinso yapamwamba mukanawona atabwera kuzasegulira koma podziwa kuti angomanga manyaka ndichifukwa abisara pheee.Zimeneziso zikuchitika kwambili ngati ntawuni tikukhara ife muno.

Zilibwino pokuti mchacha si MP wathuso akapume ifeyo watilephera ndi mchacha osati Malata.

Tiyeni timuvotereso Malata ndikudziwa akagwira ntchito ndi mai THOM NAVICHA mmudzi muzaza zitukuko mbweeee.

MALATA WOYEEEEEEEEE

13/05/2024

Anthu amene munapita kujoni muzaka zilimmusizi muzibwerako inuyo ndiomwe mukupangisa kuti Ana athu omwe apita kumeneko azisowa ntchito ....Adandaura motero azimayi ammudzi mwachisinkha
2010
2011
2012
2013
2014
2015
2016
2017
2018
2019
2020

MFUNDO ZAINE KHANSALA FANUEL  KHUZUPA NDI IZI๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡ misewu imangidwe msewu  wa misale, msewu waukulu kuyambila pasaikonde ku...
01/05/2024

MFUNDO ZAINE KHANSALA FANUEL KHUZUPA NDI IZI๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
misewu imangidwe msewu wa misale, msewu waukulu kuyambila pasaikonde kuseseleka kukonza Monse molakwika mpaka kwa mlenga. ziwaniso kuti izizizapangisa anthu kupeza ntchito komaso buliji PAKASAMBWE PANKHATHE komaso pamagazido pa MAPELERA Ana akumavutikaso popita kusukulu kumapanga.
ZAULIMI = kasambwe,magazido,manyali misinje yabwino tizayigwirisa ntchito pazaulimi mudzi wathu kuti utukuke:
ZIPATALA = chisinkha,kasaira,zimbili,nsenga ndimadera abwino kumbali yachilichonse koma mpakana Lero ziipatala kulibe sindifuna kukonza ma clinic ayi koma kumanga zipatala.
MAPHUNZIRO.. chifukwa Sogolo labwino liri mmaphunziro ndipo ndimaphunziro titha kugonjesa chilichomse tizaika ndondomeko kuti ana athu aphunzire zamaluso amanja kuti azakhare ozimilira paokha pambali pobweresa sukulu ya zasecondary yathu yathu komaso tizakhala ndithumba yachinyamata chifukwa achinyamata ambiri akulowelera chifukwa chakusowa zochita.

POMALIZA tikhalanso ndithumba yamakalamba amenewa ndiye manifesto amene ndakhazikisa mukandisankha.

zikomo kwambiri chifukwa chasapoti yanu ndimakunyadirani.

Anthu amuudzi musamumvere malata ndipo osamuvoteraso tawonani imeneija ndi buliji? Thandala ngati imeneija?Ineyo mukango...
28/04/2024

Anthu amuudzi musamumvere malata ndipo osamuvoteraso tawonani imeneija ndi buliji? Thandala ngati imeneija?

Ineyo mukangondisankha ndizamanga bridge yokuti olo truck izizadusa. Malata watipusisa kwakwana.

Khuzupa woyeeeeeeeer

Ife kuyankhura zambili ayi koma kuchita zowoneka ndimaso.Ine mukandisankha ndukuuzani kuti Muyembekezere zinthu izi zama...
28/04/2024

Ife kuyankhura zambili ayi koma kuchita zowoneka ndimaso.

Ine mukandisankha ndukuuzani kuti Muyembekezere zinthu izi zamakono๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

Bridge
School m***a kuona kuti chisinkha school ndiyachikare
Magetsi otchipa
Chipatala chachikulu osati clinic.

Nde inuyo musawamvere enawa muvotere ineyo.

Watero
Shadow Khansara Chipiliro Dowesi

Uthenga ukumamdipeza komanso ndikumaona mma Facebook kuti pali anyamata ena ammudzi muno akufuna kutimira ukhansara koma...
28/04/2024

Uthenga ukumamdipeza komanso ndikumaona mma Facebook kuti pali anyamata ena ammudzi muno akufuna kutimira ukhansara koma ine sindikutekeseka.

Aziwe kuti ukhansara sintchito yophweka pajatu sitima imaphweka akamayendesa wina watero.pakali pano ndamaliza zokambirana ndi mayi Thom Navitcha kuti tigwilire ntchito limodzi.

Nde muwauze omwe akuti azayimira u khansarawo kuti sizophweka ineyo kundigwesa .... watero Prince Malata.

Atafusidwa pa zazitukuko zomwe wachita mmudzi wangotiuza kuti sixofusaso bridge ndi ija, magesi ndi aja pakali pano nsewu watala ukubweranso.

Malata walavura khala lamoto

23/04/2024

Kuno kwavuta mayiake a ulenje amwalira ndipo ayikidwa lero koma zikumveka kuti anamenyedwa ndi mayi wina chifukwa sanapereke Thumba la sacco.

Njala itionesa usilu kumudzi kuno

Address

Chisinkha Village TA Mphuka
Thyolo

Telephone

+265884025660

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zochitika Mwa Chisinkha posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category