Comrade Hartembo

Comrade Hartembo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Comrade Hartembo, Grocers, Mwambo, Zomba.

25/11/2024

We working hard, spend wisely but still our families struggling in financial crisis 😔

10/11/2024

Ndikungomva

Mwanayo mwanayoo
Aaayeee!!
Mwanayo mwanayoo
Mwana ndi mwanaaa!

Cha Kukamudzi Stadium ku kodi mwati kwachitikanjii?😁

10/11/2024

Dzulo ndimkangoova;

Mwanayo mwanayoo,
aaayeee!

Mwanayo mwanayoo,
Mwana ndi mwanaaa

Kodi chinachitika ndi chani ku Bingu Stadium k⚽?🤭

08/11/2024

Be Focus,
Work hard.

Be Strong,
Pray hard.

02/07/2024

🇲🇼Osayankhula chomwe sukudziwa.
🇲🇼Osayankha chomwe sunachimvese.
🇲🇼Umboni waufupi koma woona umaposa kulongosola nthawi yaitali koma zaboza.
Happy independent month 🇲🇼

27/03/2024

Liwiro lilibe ntchito ngati sukuziwa komwe ukupita.

Address

Mwambo
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Comrade Hartembo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category