Editor de foto e vídeos com coll

Editor de foto e vídeos com coll Informações para nos contactar, mapa e direções, formulário para nos contactar, horário de funcionamento, serviços, classificações, fotos, vídeos e anúncios de Editor de foto e vídeos com coll, Mercearia, Tetê, Tete.

08/07/2023

Amene anfuna funa mulungu adzamupeza
Usiku wuno nikufuna Funa tulo tabwino mavumbulutso ochuluka pa moyo wanu,, ngati nanu mufuna zichitika monga mwa khumbo lanu

07/07/2023

Momwe zikhalila , kwa yinu amene muli ni wana akalakwitsa nkhope yanu yimamupatsa mantha mwanayo ,, sizitanthawuza kuti sakuyenela chikhululuko koma mukufuna ayidziwe njila yoyenela, kaya nikulondola? Ngati nikulondola mulunguso sanakwiye nanu akufuna mukhale wokhulupilika,,

07/07/2023

Masana wano muwayitanileko adzanu ku página kuti nawoso akadzinvele wokha momwe mulungu awakondela ,,,talonjezani kuti mutelo,,
Ndipo ngati angasandulike mtima chifukwa cha yinu mudzalandila modzadza ni atate wanu wa 'mmwamba..

07/07/2023

Wana wa mulungu sakhumudwa mpakana dzuwa kulowa kumakhululuka mwachangu ,, ndipo nanu mudzalandila chikhululuko mwachangu

06/07/2023

Tili ni mbili yimene tinali nayo tisanayambe utumiki , ndipo pali njila zambili zimene zinatipangitsa kuti tidzipeleke kwa yesu ,, lelo ndife odala kupanga mbali Ya tupi la yesu moyo wanu uli odala,,

Mwina muli opanda chiyembekezo ni zomwe pa moyo wanu mukudutsamo,, mukudzinva kuti simulingati crédito kapena ma mb,,mwi...
05/07/2023

Mwina muli opanda chiyembekezo ni zomwe pa moyo wanu mukudutsamo,, mukudzinva kuti simulingati crédito kapena ma mb,,mwina mukudzinva kuti muli ni ka nthawi kochepa musataye chiyembekezo tawonani yobu 2,1,13..
Timanva zowawa koma kumapeto kwake timasanduka agonjetsi yobu anapilila ndipo anawina chipambano yinuso mukhoza kupambana ndipo mupamba

05/07/2023

Mtendele wambuye wathu yesu cristo nikupatsani kose kumene muli mawa muno mwasankhidwa Ndi kupatsidwa mphanvu kuti mukasiye uthenga wabwino , tilipo angati amene tili okodzeka
A_vite nyirenda mwakodzeka?
A_xady mwakozeka?
A_bush mwale Mwakodzeka?
A_marth nyirenda mwakozeka?
A_alinafe wa dickison mwakodzeka?
A_Rhoda yakobe masache mwakozeka?
A_fretchen s nthini mwakodzeka?
Kodi naga yinu a _Alice kaunda mulipo Mulendowu ni wenanu mutipo chani za ulendou....

05/07/2023

Amene wakwanitsa kuwelenga mau awa nichifukwa choti lelo wakondeledwaso ndi kupatsidwa mphotho ya moyo ,nuwona kuti ali ni cholinga ni moyo wanu
_Pamene banja lanu ludalitsika chimwemwe chimadzadza mumasaya mwanu simuli woyenela kulila chifukwa amene mumtumikilayo ali mwini wa zose zapadziko kuphatikizapo yinuyo, muwawuze adzanuwo kuti mulungu amawakonda

04/07/2023

Como vocês estão nesta tarde

04/07/2023

Abel ndi Caim
adanva mau amodzi koma kavedwe ka kuzama kwake kadali kosiyana, mulungu sanvana ni mutu koma yinde ni mtima wagwilo

03/07/2023

MATEYU 6:1 Yang'anirani kuti musachite zolungama zanu pamaso pa anthu kuti muonekere kwa iwo; pakuti ngati mutero mulibe mphotho ndi Atate wanu wa Kumwamba.

Endereço

Tetê
Tete

Telefone

+258872949540

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Editor de foto e vídeos com coll publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Compartilhar

Categoria