IKNOW YOUR NAME

IKNOW YOUR NAME Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from IKNOW YOUR NAME, Grocers, South Africa na Malawi, Johannesburg.

Pamene Mwakhalapo✍️ tiyeni tiphunzireko mu ka nkhani aka.Mercy : hie beaGibo : hie honeyMercy : bohGibo : bohbohMercy : ...
25/09/2025

Pamene Mwakhalapo✍️ tiyeni tiphunzireko mu ka nkhani aka.

Mercy : hie bea
Gibo : hie honey
Mercy : boh
Gibo : bohboh
Mercy : ubwera lero?
Gibo : ayi ndipita kudimba
Mercy : chabwino! Koma dress lija wandigulira?
Gibo : ayi, udikire kaye ndipeze ganyu wowumba njerwa.
Mercy : chani? Mpaka kuwumba njerwa?
Gibo : eyaka, ndikakupasa ndalama ndimakhala ndagulitsa njerwa or foni ndidakugulira ija ndinkapelekera matope.
Mercy : iiiiii chabwino darling.

*After 3 months*

Mercy : hello my boy
Gibo : hello hun
Mercy : tikumane chonde
Gibo : ok chabwino
Mercy : kwathu andipatsa 200pin kuti ndikagule zovala koma ubwere udzatenge ndalamayi kuti uyambire
Ka business mwina upumeko
yowumba njerwayo.
Gibo : eeeeh ndalama yoseyo?
Mercy : eya dear dzatenge
Gibo : zikomo kwambiri my love

* After 6 months*

Makolo ake a Mercy adamwalira pa ngozi yagamoto, apa nkuti Gibo akupangabe business yake ndipo zinkamuyendera kwambiri
choncho adatenga udindo wolipira school fees ya Mercy mpaka kukoleji ndipo ankathandizaso abale ake a Mercy.

*Phunziro*

Amuna azanga tiyeni tizikhala a chikondi, okhulupilika komaso olimbikira pa njira yomwe imatipatsa ndalama.
Si akazi ose omwe amafuna ndalama, ena alipo amene amangofuna chikondi ndi kukhulupilika kwathu.
Choncho kudzichepetsa ndikwabwino osati kumana kuti mumagwira ntchito yapamwamba muzasemphana ndi madalitso.

Akazi inu, musamunyoze mwamuna chifukwa choti alibe ndalama moyowu ndiwozungulira sudziwa wodzakugwira nkono mawa lino chofunika ndichikondi chuma chimachita kubwera.

Anthu Ambiri Amadana ndi Mau A Mulungu Koma kukakhala Za dziko Monga Chuma ndi Zina zambiri amapanga follow komaso Cheya Koma Mau A Yehova Ayi😭 Ambuye ivani kulira
😭😭😭😭😭😭😭
Kwamwana wanu chonde mupatseni chomwe akufuna ngati akwanitse kulemba kuti Amen Ndikupanga follow 🤲🤲🙏🙏

Mukadina malemba awa 👉 Tilalike Uthenga ndikupanga follow komanso sheya Ngati ukuona post iyi

Zikomo powelenga ❤️

16/09/2025

*IMPORTANT*
*AMALAWI NONSE OKONDA DPP*

Chipani chachikulu cha DPP chikuziwitsa Amalawi onse ndi masapota onse kuti panopa mukhoza kuwaziwisa akulu Akulu akuchipani ngati mungaone Vuto lililonse kudela Kwanu pachisankhochi.

Uthenga wanuwu uzatengedwa serious komanso tizasunga chinsinsi chanu

Aliyense ndi monitala kuti Zisankho zathu zikhale zabwino

Manambala mukafuna Kuimba ndi awa 24/7

0894342297
0987712554
0990803124
0990803151
0997124416

Manambala mukafuna kutumiza pa WhatsApp ma video Kaya zithunzi ndi awa

0980524209
0885035224

*Aliyense apange share uthengau*

Address

South Africa Na Malawi
Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when IKNOW YOUR NAME posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category