16/03/2026
Mayi mpinga njira zomwe achitazi sizololedwa komaso a police sanatsate malamulo awo pachifukwa ichi amayi onjatidwawo payenera k*t abaleawo apite kumabugwe k*ti athandizidwe moyenera chifukwa apa sanatsate malamulo kodi makolo pazomwe zachitikazi mwaganiza bwanji chifukwa aphwanya ufulu wa mayiwo