Nkhan zokoma kuziva

Nkhan zokoma kuziva Don't forget like ths page kut zambili zasakuphonyen

15/11/2022

Pamene tikuyandikila December wina avekele uzandifuna pa24 πŸ˜‚πŸ˜‚ ndiwe mpunga wanyama kapena fantaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

11/11/2022

Anthu obweresa mayeselo ukapandakuwasatila zochita zawo umakhala ndimtendele wamuntima

08/11/2022

🌧🌧🌧🌧🌧🌧 S A today prtoria East

06/11/2022

Whu are not know gan bos is number1 artist in malawi ithnk today every bleday we know πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

05/11/2022

We are saying what tumbuka after gfit soya pces? πŸ˜›πŸ˜œπŸ˜œπŸ˜‚πŸ˜‚

05/11/2022

Mwazuka bwanji guys kuno watisamalila yawe sitiziwa kwanuko

03/11/2022

Nthawi zina kukamacha ngati kusachetu πŸ˜‚πŸ˜‚

02/11/2022

Muk*ti bwanji ndinkan mukuvaz zokhuza kudayinila zopusa apule anu achakwela

30/10/2022

Osamadanda k*ti mulibe ndalama chiyambi ndiye chimavuta khalan ochilimika munthawi zose muzakhala ngat anebawo palibe anabadwa ndindalama zimachiti kubwera munthawi yake bola osaziyanganila pasi kumangopemphela kwayawe zizakhala better

27/10/2022

Pepan guys osamadabwa some times tikamachita mwano vuto ndilot azanufe tinakula movutika ngat chigumu pamwamba moto pasiso moto πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

25/10/2022

Ukhale ndika life kosaziwa kufusila ndiye mwamwayi uzakhale ndikachibwez kofusililidwa asangotitu bea ndikufuna yaku salun πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

23/10/2022

Chidziwiso mukawona zizindikilo izi πŸ‘‡
1 kufooka
2 kuuma milomo
3 kumangot zungulilu zungulilu kusowa kopita
4 kuwawa mkamwa
5kazuwa koboweka

Musachedwe mupeze chakudya imakhala njalaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Send a message to learn more

Address

Cullinan
Pretoria
350663

Telephone

+27785453422

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhan zokoma kuziva posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category