Chiudya

Chiudya Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chiudya, Grocers, Linaria Street, Vereeniging.

07/06/2026

Lero tipange zapanga chi Sunday

06/06/2026

🥺🥺🥺🥺🥺

Khoti lapereka chilolezo chomanga Ngizwe Mchunu pambuyo poti apezeke wolakwa pa mlandu wosalemekeza khoti chifukwa choph...
05/06/2026

Khoti lapereka chilolezo chomanga Ngizwe Mchunu pambuyo poti apezeke wolakwa pa mlandu wosalemekeza khoti chifukwa chophwanya lamulo la khoti lokhudza mawu onyoza mtsogoleri wa EFF, Julius Malema.

Izi zikubwera pambuyo poti Ngizwe Mchunu adapepesa kwa Malema ndikulonjeza kuti sadzabwerezanso kunena zinthu zomunyoza. Nkhaniyi inayamba pamene Malema anapita ku khoti la North Gauteng High Court atamva kuti Ngizwe ananena kuti Malema analandira ndalama zokwana R60 miliyoni kuchokera kwa ogulitsa mankhwala osokoneza bongo aku Nigeria.

Ngizwe ananena izi pa interview yomwe anachita pa 28 April. Koma atalephera kupereka umboni wa zonenazo, khoti linagamula pa 19 May kuti mawu ake anali “osaloleka komanso onyansa,” ndipo linamulamula kuti achotse zonenazo ndi kupempha chikhululukiro.

Mu kalata yake yopempha chikhululukiro, Ngizwe — yemwe amadziwikanso ngati m’modzi mwa atsogoleri omwe amalimbana ndi osamukira m’dziko mosaloledwa ku South Africa — adabwezera mawu ake ndikupepesa.

Olemba nkhani ndi yemwe uja

05/06/2026

Anthu awa atimaliza basi eeeee

04/06/2026

Zithu azaipa pa theba guys

29/05/2026

@

29/05/2026
28/05/2026

Ndie mwati kukulubani zathapo bwanji
🤣🤣🤣🤣🤣

Man U fans 😜😜😜😜
27/05/2026

Man U fans 😜😜😜😜

Address

Linaria Street
Vereeniging
1831

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chiudya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category